A.S . Emanuel phiri Mlakatuli

A.S . Emanuel phiri Mlakatuli Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from A.S . Emanuel phiri Mlakatuli, Poet, Ntaja, Machinga.

Siose amene chingakuyanjeni chikondi enanu unakuyanjani umbeta.πŸ™„πŸ™„
04/09/2024

Siose amene chingakuyanjeni chikondi enanu unakuyanjani umbeta.πŸ™„πŸ™„

With Legend of poetry
28/04/2024

With Legend of poetry

17/02/2024

Valentine

Idabwela Valentine ngati mulendo olonjezedwayo.
Mwe!!!! Ena kusekelera mulendo
Posaziwa kuti mawa libalanji.
Ena mkumafusidwa kuti anu achikondi alikuti poti mulendo wa leroyu amafuna kutiona tili awiri awiri.

Vuuu adapita mulendo mkuwasiya
wasiya atakhumata anga nkhuku za chitopa ena adawasiya ali ndi mimba akukanidwa ndi wao wachikondi ndithudi mulendo wa Valentine anabweleresa chikulirano pamaso pa salamankhwe.

Tidapitilira kuva zosatila za mulendoyo zomwe zikatikankhila kuti tisafuneso kuzakondwera naye mu tsiku lina ndithudi tiva zokuthaitha
Kuti chingwe chochosa moyo chilipakhosi pa mwana wa neba ati sakuonaso chifukwa chokhala ndi moyo pakuti wachitisidwa manyazi pa maso pa mulendo otchedwa Valentine Poona wake wachikondi atatengana ndi wina eish mulendo.

Ena tingova akuti ayi sitikumufuna kumuonaso
tikawafusa chifukwa ninji? ati anawabalitsa moyo wao ngati a ndale ndithudi mulendo yo adafiika pameto utisiya ndi misozi anga a nafedwa.

A.S . Emanuel phiri Mlakatuli






mukuoneka

19/12/2023
18/11/2023

Malawi tingogwira patima uyu akudwalika koopsa akufuna mtera.

18/11/2023

πŸ•·οΈπŸ•ΈοΈ tauzaso kuti athane ndi Chakweratu ooohπŸƒπŸƒ

18/11/2023

Tilipano pa maliro amene wamwalira sikumuziwa Chiwamba

18/11/2023

Komano mubwelera liti Ku thebako kunotu muzangova mtundu wanu ose watha ndi chakweratu. Ooooh

18/11/2023

Inuyo ameneo kutikana ife mkukwatira ndi chidala chamowa ngati chimene chija ayi zikomo .

Address

Ntaja
Machinga

Telephone

+265986220550

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when A.S . Emanuel phiri Mlakatuli posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category