Nyombe Media

Nyombe Media Promoting Malawian businesses 🇲🇼 | Local news & talent | Advertise with us”
(1)

CA$INO to perform at Gwamba's Concert in August 🔥
05/06/2026

CA$INO to perform at Gwamba's Concert in August 🔥

*Yapeza witi nkhani ija kuno 😄😄😄😄🤣*
05/06/2026

*Yapeza witi nkhani ija kuno 😄😄😄😄🤣*

 Authorities have arranged buses to transport over 500 Malawians affected by recent xenophobic attacks back home.The bus...
05/06/2026



Authorities have arranged buses to transport over 500 Malawians affected by recent xenophobic attacks back home.

The buses will carry the affected Malawians to the Malawi Embassy in Pretoria as part of repatriation efforts.

The transportation has been organized to bring Malawians from South Africa back home.

The swift government response follows appeals from Malawians stranded in South Africa seeking assistance to return.

Amalwi omwe anathawira ku kleinmond hall western cape anyamuka kupita ku Johannesburg mothandizidwa ndi malawi Embassy, ...
05/06/2026

Amalwi omwe anathawira ku kleinmond hall western cape anyamuka kupita ku Johannesburg mothandizidwa ndi malawi Embassy, kumene akadikire ma bus omwe boma litumize kuti azipita kumudzi.

Sidenote:Akadikira Ku Johannesburg osati apita straight Ku Malawiii.👂👂👂

Ati Mzungu amamupempha Mayor ndalama ya Cape stars__Koma anthu mumayankhulitsa Eeeh 🙌
05/06/2026

Ati Mzungu amamupempha Mayor ndalama ya Cape stars__
Koma anthu mumayankhulitsa Eeeh 🙌

Breaking News Wa Bakili Muluzi TV wamung'alula kamangila akuti ku school anapita Kuja ku Island akuti anamuwida kale kal...
05/06/2026

Breaking News

Wa Bakili Muluzi TV wamung'alula kamangila akuti ku school anapita Kuja ku Island akuti anamuwida kale kale atalemphera mayeso zochititsa manyazi zinja akuti matukutuku amapanga pa Facebookwa amafuna yolipilira rent.

BMT anapitiliza kunena kuti Kamangila akumanyoza anthu kuti dziko la Island adzimuvera chisoni kuti amupatse asayilamu yoti asachoke ku island ati poti moyo wake uli pa chiopysezo. Kutengera ndi wa BMT akuti kamangira atapanga apply za asayilamu ku Island akuti anamukanira pakuona kuti moyo wake suli pachiopysezo poti anthu omwe iye amawang'alula samuyakhaa.

Ati pompano tiva Kuti amupanga depoti

Mwachidule akuti Kamangila alibe pepala lilirose ndi chimodzi modzi ndi wa MSCE holder.

Mutharika addresses Catholic concerns in Malawi President Peter Mutharika's administration says it has taken note of con...
05/06/2026

Mutharika addresses Catholic concerns in Malawi

President Peter Mutharika's administration says it has taken note of concerns raised by the Catholic Church in Malawi on governance, the economy, security and public service appointments.

FAMOUS [INTERLUDE] out now 🔥
05/06/2026

FAMOUS [INTERLUDE] out now 🔥

Famous (Interlude) off my upcoming album, ENJOY!

Mmazidziwa nsomba izizi
05/06/2026

Mmazidziwa nsomba izizi

05/06/2026

Address

Area 24
Lilongwe
132-567

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyombe Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category