Mikoko Entertainment

Mikoko Entertainment Arts and entertainment
(4)

Apapa sizinayendeNkhani ya NYONDOYI Mwati Date lake lenileni ndi liti? Osanama ma Editor atibalalitsa💔😥
20/06/2026

Apapa sizinayende

Nkhani ya NYONDOYI Mwati Date lake lenileni ndi liti? Osanama ma Editor atibalalitsa💔😥

Anthu okhala ku Ndirande ku Zion pa Sunday anapha Christopher Kamzati pomuganizila kuti ndiwokuba. Mkazi wake anangodabw...
20/06/2026

Anthu okhala ku Ndirande ku Zion pa Sunday anapha Christopher Kamzati pomuganizila kuti ndiwokuba.

Mkazi wake anangodabwa kuti amuna akewa sakuwlbwera kunyumba. Ndiye anadziwitsa makolo a Christopher. Kuyamba kufufuza kenaka kumazazindikila kuti thupi la mwana wawo liri ku mortuary ya Chipatala Cha QUEENS.

Christopher amakhala kuno ku Ndirande kwa Safalawo pafupi ndi chigayo chaa window.

Ma report omwe tapeza kuchokela ku Zion ndi okuti Christopher akubwera kuchoka koyang'ana msganyu, amadutsa njira zachidule za mu Zion. Ndiye anazamva kutentha m'mimba zomwe zinamupangitsa kulowa mu toilet ina koma sanapemphe permission.

Za ku toilet ko zinatheka ndithu. Koma potuluka eni toilet anamuwona ndikuyamba kukuwa kuti awona wakuba. Christopher anayesera kuwafotokozera awawa kuti iyayi ine si mbava koma sizinamveke. Ndiye gulu linafika. Atamupanga search anamupeza ndi mpeni. Komanso bunch ya ma key.

"Mpeni wo ndimayenda nawo ngati chozitetezela ku ana amasikini chifukwa anandipangapo chipongwe nthawi Ina yake." Anayankha Christopher atafunsidwa. Koma zinawoneka kuti sizinamveke.

Anthu wo anamupondaponda mpakana kumupha.

A police anadziwa Monday mmamawa kuti kwaphedwa munthu ndipo anakatenga thupi lake kukasiya ku mortuary.

Pali video yomwe inajambulidwa ya izi koma polemekeza Christopher sitipanga post.

Pangani Follow Mikoko Entertainment ngati mukufuna kumva zambiri 🙏

Ubale pakati pa dziko la US ndi South Africa wasokonekera pambuyo poti boma la US lalengeza ndondomeko yoti lisiye kuper...
20/06/2026

Ubale pakati pa dziko la US ndi South Africa wasokonekera pambuyo poti boma la US lalengeza ndondomeko yoti lisiye kupereka ndalama zothandizira mapulogalamu a HIV/Aids m'dzikolo. Ena mwa maganizo omwe aperekedwa ndi akuti dziko la South Africa lalephera kuteteza anthu ochepa achizungu amtundu wa ma Afrikaner.

Kufikira m'chaka cha 2025, dziko la US lakhala likuthandiza South Africa polimbana ndi kachilomboka kudzera pa ndalama zokwana 400 million dollars pachaka kudzera m'bungwe la Pepfar.

Dziko la US lati South Africa ndi dziko lomwe lili ndi chuma chapakati, choncho lili ndi kuthekera konse kodzipezera lokha ndalama zoyendetsera mapulogalamu ake a zaumoyo.

Komabe, akuluakulu a zaumoyo ku South Africa ayankha kuti, ngakhale sadadziwitsidwe za chigamulochi, koma akhala akugwira ntchito kale pa ndondomeko yodziyimira pawokha.

Pakadali pano, dziko la South Africa ndilo lili ndi chiwerengero chachikulu kwambiri cha anthu omwe ali ndi kachilombo ka HIV pa dziko lonse lapansi, pomwe anthu opitilira 8 million ali ndi kachilomboka.

Follow Mikoko Entertainment for more information.

20/06/2026

Pachitika Mistake aah🤣🤣🤣

20/06/2026

Tilipo angati Amene taona kuwala Kwa tsiku la lero pa 20 June, 10 secs yokha Thokozani Mulungu Kumwamba 🙏

19/06/2026

mutawina 5 million lero mungatani nayo???

Ngati zimatheka kukumana kwinako ndee Kuti akumananso..Rest in peace azibambo 🕊🙏
19/06/2026

Ngati zimatheka kukumana kwinako ndee Kuti akumananso..

Rest in peace azibambo 🕊🙏

Sad News💔Katswiri wojambuka zinthuzi, Ras Kasengwa wamwaliraMay His Soul Rest in Peace 🕊️
19/06/2026

Sad News💔

Katswiri wojambuka zinthuzi, Ras Kasengwa wamwalira

May His Soul Rest in Peace 🕊️

19/06/2026

Sim'mene kulili Ku TikTok

Anthu apwetekana 💔😭👇

19/06/2026

Kafukufuku wa Ndege wabweletsa mapokoso koopsa.

check Ku comment section

Address

265
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mikoko Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share