Mtolankhani Opanda Chisisi

Mtolankhani Opanda Chisisi 📰 Mtolankhani Opanda Chisisi. Choonadi chathu, mawu athu, nkhani zathu.
🔎 Timafufuza • Timafotokoza • Timanena zoona.

Galimotoya mtundu wa Minibus yagwa pa Thabwa pomwe imachokera ku Blantyre kupita ku msanje.Anthu ochuluka athamangira na...
22/08/2026

Galimotoya mtundu wa Minibus yagwa pa Thabwa pomwe imachokera ku Blantyre kupita ku msanje.
Anthu ochuluka athamangira nawo ku Chipatala cha Chikwawa.

Source: Zodiak

Akutero graduate wa ku UNIMA🤣🤣👇"Mu nyengo imene ena amona ngati tikukokomeza koma ayi ndithuMa yearo nonse akuwidani 😂"
22/08/2026

Akutero graduate wa ku UNIMA🤣🤣👇

"Mu nyengo imene ena amona ngati tikukokomeza koma ayi ndithu

Ma yearo nonse akuwidani 😂"

Sad news💔👇Copied and pastedFirst year, first Semester Students, Catherine Mvula from Mzimba watisiya atawombedwa ndi Gal...
22/08/2026

Sad news💔👇

Copied and pasted

First year, first Semester Students, Catherine Mvula from Mzimba watisiya atawombedwa ndi Galimoto pa Ginery Coner masanawa when she was crossing kuti akumane ndi Bambo Ake omwe panthawiyo amachokeera ku Mzuzu kuzamupasa Zofunikira...

Rest in peace Catherine💔🙆‍♀️

Even ma supporter sakuvetsabe💔👇👇
22/08/2026

Even ma supporter sakuvetsabe💔👇👇

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mtolankhani Opanda Chisisi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category