Soldiers IN Christ CHOIR

Soldiers IN Christ CHOIR It is a group of young and energetic men who sing for the LORD. The group started while at Nkhoma College of Nursing and Midwifery

Good morning everyone Mulungu akutsogolereni pa zonse muchita
04/11/2025

Good morning everyone

Mulungu akutsogolereni pa zonse muchita

03/11/2025



Tsiku lanu likuyenda bwanji

03/11/2025

imasautsadi moyo, koma aaa nzotheka , Mulungu amakupatsa njira yobwenzera.osachotsa moyo.
Nyimbo zathu 10 tumagulitsa pa Whatsapp 5 pin yokha. 0998666931
Pompopompo

Khalani ndi tsiku lopambana, ambuye akudalitseni

Two of three Men behind the Basses of soldiers in Christ songs, like   All the songs  and
02/11/2025

Two of three Men behind the Basses of soldiers in Christ songs, like


All the songs
and

02/11/2025


Nyimbo imodzi ya new one yomwe ili mu album ya

Tingaloze amene anayambitsa nyimboyi pa chithunzicho?

02/11/2025



Tili Nako kokazipereka?

From chair WA soldiers, kuyese zida

02/11/2025

MATTHEW 6:33
But seek ye first the kingdom of God and his righteousness and all these things shall be added unto you.

Kumapemphera ndi kupempherelanatu kumeneko.

26/10/2025

Mwakapemphera kuti lero!

Umu ndi mmene kwaya inayambira...maimbidwe ake anali amenewa komwe ku school ya za unamwino ku Nkhoma mu zaka za pakati pa 2015 mpaka 2019.

M***a kuonera kanema wake wa nyimbo imeneyi pa YouTube titatha kujambula pa link ili mmusiyi.

https://youtu.be/7-dEt_DplSo?si=hEYRCITvskJdEBmK

23/10/2025

Mwaswera bwanji kumeneko?

NKHAWAZI TIMUPATSE YESU

Today, we are celebrating the birthday of our Publicity Secretary.Join us in wishing him a happy and fulfilling year ahe...
22/10/2025

Today, we are celebrating the birthday of our Publicity Secretary.

Join us in wishing him a happy and fulfilling year ahead.
Happy Birthday, aChisale! 🎉

Thanks for being a top engager and making it on to my weekly engagement list! 🎉 Steve Masenda, Vannie Vio, Nellie Jonelj...
21/10/2025

Thanks for being a top engager and making it on to my weekly engagement list! 🎉 Steve Masenda, Vannie Vio, Nellie Joneljollie Ba-Chi, Gift Makolo, Jesca Mhango, Chakwera Chakwera Banda, Alex Mwale, Neph Banda, Frank Emmanuel, Mable Felix, Philip M Sizaliyo, Jackson Leckford, Chisambi Eliza Chisambi, Malopa Winfred, Violet Manondo, Eneless Magomo, Lucy Chauma, Constance Mtongola, Mathero Kachitsamba, Sellah Tumeyo Nkhata, Monica Abrahm, Cathy Goodwell, Loveness Mulole, Jessica Simango, Faith Chiwaula, Titus Samalani Chingapa, Chris Wa Nandewe, Flvme Scott, Eresi Kaselo, Latima Boston Mbewe, Biglet Henry, Moffat Kanyoza, Mark Farayi, Gift Njoka, Chancy Taombe, Micah Kalimbira Banda, Ulemu Mbewe, Mathews B Dzonzi, Memori Kandeu, Petter Gomiwa, Ignasio Chiphale Major, Mack Lingard Mlenga, Christina Kazembe, Carloleen Chinganyama, Davie Jailos, Nalisiziy Mazoni, Josephy Ngozo LG, Chemlera Chemlera, Dazzon Blessings, John Khwethe Kalibwanji Chisomo

19/10/2025

Umu ndi mmene zinalili lero ku mpingo wa Strand CCAP, Capetown - South Africa, pansi pa Synod ya Nkhoma omwe ukutsogoleredwa ndi abusa a E.K Mseche.

challenge accepted.

Over to you all our followers. Kwanuko mukhoza kuikometsa motani?

Address

Nkhoma Synod
Lilongwe

Telephone

+265882935649

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Soldiers IN Christ CHOIR posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category