Menai facts

Menai facts Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Menai facts, Arts and entertainment, Area18 A, Lilongwe.

21/04/2026
Nsanje yotani. Finally akwanitsa kulowa ku kitchen top up  kuwalondola akazi awo
14/05/2025

Nsanje yotani. Finally akwanitsa kulowa ku kitchen top up kuwalondola akazi awo

zikafika apa mmatani😅
08/05/2025

zikafika apa mmatani😅

zamalove😂
08/05/2025

zamalove😂

😂 artist CCharisma Madnessapa ukutipo chani😂😂
08/05/2025

😂 artist CCharisma Madnessapa ukutipo chani😂😂

Izi ndizomwe ayamba ma MG1,akumalizani mukapanda kusamala ma Baddie
19/04/2025

Izi ndizomwe ayamba ma MG1,akumalizani mukapanda kusamala ma Baddie

Mayi yemwe akuti wapolisi wina pa polisi yaying'ono ya Chigodi kwa Santhe m'boma la Kasungu anamuvulaza wati akufuna chi...
16/04/2025

Mayi yemwe akuti wapolisi wina pa polisi yaying'ono ya Chigodi kwa Santhe m'boma la Kasungu anamuvulaza wati akufuna chilungamo chioneke pa nkhaniyi.

Mayiyu yemwe amachita bizinezi yogulitsa keke m'deralo Ivy Selemani wazaka 42 wati wapolisiyo pamodzi ndi apabanja pake anamumenya pomuganizira kuti amafalitsa nkhani zabodza za banjalo.

Mayiyo watiuza kuti iyeso ndi wodabwa kuti nkhani zomwe akuti amafalitsazo ndi ziti ndipo kuti anthuwa anangoyamba kumumenya atakumana naye panjira ali pa ulendo wokachita bizinezi ku nyumba ya wapolisi wina yemwe ndi neba wa wapolisi yemwe anamuvulazayo.

Pakadali pano wapolisi yemwe akumuganizira kuti anavulaza mayiyu sanayankhulepo pa nkhaniyi, koma mayiyu wati anakamuneneza kale kupolisi ya Chigodi-yo, ngakhale kuti anamuopsyeza kuti akatero, amangidwa.

Mneneri wa apolisi m'bomali a Joseph Kachikho wati pakadali pano sangayankhulepo zambiri pa nkhaniyi.

Koma wapampando wa mabungwe omwe siaboma m'bomali a Braxton Banda wati ngati mabungwe atsatira bwino nkhaniyi kufikira chilungamo chitayenda ngati madzi.

Mverani KCR pa 107.6MHz kapena pa p3

Malonda awa Kodi ndi azimayi okha?
13/04/2025

Malonda awa Kodi ndi azimayi okha?

2nd princess miss albinism Malawi.Graduated from the university of Malawi with a bachelor's degree in Social science Soc...
13/04/2025

2nd princess miss albinism Malawi.Graduated from the university of Malawi with a bachelor's degree in Social science Social work with credit. and a first year law student at The Catholic University. Machine Mary Seunda🔥🙌🏻

Koma blesser mkazi akadya ndalamazo sizoti muziphwanyaso mutuwo iyayi 😂
13/04/2025

Koma blesser mkazi akadya ndalamazo sizoti muziphwanyaso mutuwo iyayi 😂

Address

Area18 A
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Menai facts posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share