08/06/2026
M.Tech Sounds ndi bizinesi yopereka za usangulutsu ndi zochitika izi:
~ Umisili pa za kuimbitsa
▪︎ Kusakaniza mawu (Sound Mixing)
▪︎ Kusintha ndi kufananitsa mawu (Sound Balancing)
▪︎ DJ (Disk Jockeying)
~ Kubwereketsa Zida zoimbila:
▪︎ Maukwati
▪︎ Bridal Shower
▪︎ Ma Send-Off
▪︎ Ma Engagement
▪︎ Ma Concert/Shows
▪︎ Zochitika za Makampani (Corporate events)
▪︎ Maphwando a Tsiku Lobadwa
▪︎ Ndi zina zambiri
~ Kukonza ndi Kuyang’anira Zochitika (Events Hosting)
▪︎ Kafukufuku
▪︎ Kukonzekera
▪︎ Kukhazikitsa (Implementation)
▪︎ Kuwongolera (Management)
▪︎ Kuwunika (Evaluation)
Lumikizanani nafe pa ma nambala awa:
WhatsApp
0990 27 18 94
Ma foni/Ma meseji okha
+265 990 271 894
+265 892 523 465
+265 892 523 467
+265 991 791 950
+265 995 211 361
Tikupezekera ku Area 23, Lilongwe, Malawi