ZA LUSO

ZA LUSO Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from ZA LUSO, Arts and entertainment, Kasungu, Lilongwe.

Music producer waiting for the Artist to send Money for The Beat 🥱😂
30/01/2025

Music producer waiting for the Artist to send Money for The Beat 🥱😂

Koma wapanga izi ELI Njuchi waziona 😂🚶 GwGwamba ChCharisma Madness😂 mota yafika dzro iyi
30/01/2025

Koma wapanga izi ELI Njuchi waziona 😂🚶 GwGwamba ChCharisma Madness😂 mota yafika dzro iyi

Ku India, ku Festival ya chi Hindu ya Kumbh Mela, imene ndinanena kuti ikuchitika mu January 2025 pomwe kumayembekezerek...
30/01/2025

Ku India, ku Festival ya chi Hindu ya Kumbh Mela, imene ndinanena kuti ikuchitika mu January 2025 pomwe kumayembekezereka kufika anthu 400 million kwapangika ngozi.

Ku Festival imeneyi, anthu a chikhulupiliro cha chi Hindu amakasonkhana pamene mitsinje itatu imakumana.

Kumeneko amasamba muntsinjemo kuti machimo akhululukidwe, achilitsidwe ndipo awone zozizwa pamiyoyo yawo.
Izi zimachitika kamodzi mu dzaka 12.

Pali chikhulupiliro chakuti Mulungu wawo anatsanuliramo moyo osatha mumtsinjemo.

Pa 28 January, anthu anachuluka kwambiri ndipo pofuna kusuntha, chinantindi chawanthu chinagwa, kupondana ndipo anthu 12 amwalira pamene 20 akulandira chithandizo ku chipatala.

Sidenote
Aliyense ali ndi chikhulupiliro chake. Ndipo aliyense amaona kuti chikhulupiliro chake nde cholondola

30/01/2025

Yavuta ndi plot ya ELI Njuchi

Onesimus Muzik chikubwela chigawenga   onesimus🔥 monday out
30/01/2025

Onesimus Muzik chikubwela chigawenga onesimus🔥 monday out

30/01/2025

*HELLOW DEAR ARTIST from MPONELA , KASUNGU , BUA , BOWE , KASESE , MADISI NDIMADELA ENA OZUNGULIRA TIKUKUDZIWITSANI KUTI SHOW YAKU MADISI IJA TASITHA DATE IKHALAKO PA 13 APRIL 2025*

apa tikupitilizabe kutolela ma pic ndimayina ama artist .tipezeni pa 0983408177 tnm 0886109454 or inbox ngati muli ndiluso lofuna kudzationetsa patsikuli..

Mukafuna mamodelo ojambula nawo video mupezeni CRETH ndipo simudzankhumudwa👇🔥
20/01/2025

Mukafuna mamodelo ojambula nawo video mupezeni CRETH ndipo simudzankhumudwa👇🔥

Asiyeni A'ba lé alowe mkati…
20/01/2025

Asiyeni A'ba lé alowe mkati…

Mwaona, Nyumba zaku American, sizimakhala ndi mpanda. Koma iwe ndi ine, oti bed yathu ndiyochita kukumbira pansi ngati b...
20/01/2025

Mwaona, Nyumba zaku American, sizimakhala ndi mpanda. Koma iwe ndi ine, oti bed yathu ndiyochita kukumbira pansi ngati bench, koma chimpanda Cha tsekera dii, Ati kuopetsa akuba, akuba angabwere adzabe bed yokumbira pansiyo? 🤣🤣🤣🤣

Bwanji by SKIP JACK link ili commentmu👇😂😂
20/01/2025

Bwanji by SKIP JACK link ili commentmu👇😂😂

No matukutuku no ma stunt koma princess ngini aku phusha🔥
20/01/2025

No matukutuku no ma stunt koma princess ngini aku phusha🔥

Address

Kasungu
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ZA LUSO posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share