Aras

Aras Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Aras, Lilongwe.

Zovuta💔💔💔Wakabaza amene anasowa muchaka   Cha 2015 nthupi lake lapezeka mukhalango ina chaku border ya malawi ndi Zambia...
12/06/2026

Zovuta💔💔💔
Wakabaza amene anasowa muchaka
Cha 2015 nthupi lake lapezeka mukhalango ina chaku border ya malawi ndi Zambia chaku chitipa, so sad 😭

Kaya zimakhala bwanji kaya
12/06/2026

Kaya zimakhala bwanji kaya

Girls type yanu apa ndiuti Aras
12/06/2026

Girls type yanu apa ndiuti Aras

RONWEN WILLIAMS goalkeeper wa South Africa wadandawula kuti maiko aku Africa sanawapatse sapoti.Tankhetsa misozi kuwona ...
12/06/2026

RONWEN WILLIAMS goalkeeper wa South Africa wadandawula kuti maiko aku Africa sanawapatse sapoti.

Tankhetsa misozi kuwona abale athu aku Africa akuspota Mexico.

Kugonjetsedwa kwathu lero sikunali chifukwa choti sitinayesetse kwambiri. Ndikukhulupirira kuti kusowa kwa thandizo kuchokera kwa anthu ena aku Africa kunathandizanso.

Africa ndi kontinenti yomwe nthawi zonse ndakhala ndikudziwa kuti imathandiza ndi kuyimirira limodzi ndi matimu ake pa World Cup kapena mipikisano yapadziko lonse, koma kwa ife zinamveka ngati zinthu zinali zosiyana.

M’malo mokhala ogwirizana, kugonjetsedwa kwathu kukuoneka ngati kwasangalatsa anthu ena, ngakhale ena omwe ali mu Africa. Zimenezi zinatikhumudwitsa, chifukwa tinkayembekezera kuti kontinenti yathu idzakhala nafe nthawi ngati izi.”

Maiko ambiri aku Africa sakuyisapota South Africa chifukwa Cha nkhaza zomwe akuchitila anthu amayiko ena ku South Africa.

South Africa yagonja 2-0 ndi Mexico usiku wapitawu.

follow Aras for more updates

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Aras posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share