Uzimu Vibes

Uzimu Vibes We promote Malawian Gospel Music ||
Call/WhatsApp 0881031858.
(7)

Koditu Soya Pieces uja amangofunika akumane ndi dolo pa moto😋.. enawa amawakanika kuphika mpake amadana naye😍🤸
23/08/2026

Koditu Soya Pieces uja amangofunika akumane ndi dolo pa moto😋.. enawa amawakanika kuphika mpake amadana naye😍🤸

Anthu ochuluka adzidzimuka atamvera nyimbo ya Melody Mijoya yatsopano yomwe akuti "I Menifest"🥰. "Kodi ameneyudi ndi m'M...
23/08/2026

Anthu ochuluka adzidzimuka atamvera nyimbo ya Melody Mijoya yatsopano yomwe akuti "I Menifest"🥰. "Kodi ameneyudi ndi m'Malawi?" Limeneri ndi funso lomwe ambiri akufunsa chifukwa nyimboyo ikumveka zawu international kwambiri. LINKS in the comments section👇

23/08/2026

Atsogo, kodi ndibwino kutenga chenji mu mbale ya chopereka kapena tidzisithiratu ku nyumba?🤔

23/08/2026

Nyimbo za Chichewa ndizabwino osamaziphweketsa ayi🥰👇

23/08/2026

Kudzukanso ndi moyo nde umboniwo. Osamazitengera chizolowezi.

GOODMORNING💥

22/08/2026

Kugona osapemphera ndi mistake yaikulu kwambiri. Satana amatha kukuseweretsa.

GOODNIGHT

22/08/2026

Eh koma nzimayi uyu ngokongola ndi mtima omwe ndipo akugwira ntchito yotamandika. Ambuye apitilize kumudalitsa kuti akatheso kufikira anthu ena ochuluka🥰👇|| Apostle Huldah 💯💪

Mwana wa Thoko Suya wapanga gala. Congratulations Victor👏👏👏
22/08/2026

Mwana wa Thoko Suya wapanga gala. Congratulations Victor👏👏👏

22/08/2026

Mwana yemwe wapatsidwa 20 Million Kwacha ya scholarship uja kufotokozapo za chimwemwe chake komanso kuthokoza Apostle Huldah ... Uyu zake zayera basi🥰

22/08/2026

Apostle Huldah yemwe ndi mkulu wa Apostle Huldah Foundation lero apereka cheque cha 20,144,000 Malawi Kwacha kwa mnyamata wa zaka 18, Naphtali Dickson, ngati mbari imodzi ya scholarship yomwe imuthandizire Naphtali pa maphunziro ake pomwe akukayamba maphunziro ku school yaukachenjede ya Chancellor College.

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Uzimu Vibes posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Uzimu Vibes:

Shortcuts

Share