Pamtondo

Pamtondo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Pamtondo, Arts and entertainment, Lilongwe.

Fare thee well Brian Banda. πŸ™Œ
08/08/2026

Fare thee well Brian Banda. πŸ™Œ

Atelala pa ntchito yawo cheteeee!
07/08/2026

Atelala pa ntchito yawo cheteeee!

Eish! Apule Chikomeni awambwandira Ali ndi Zaza mgalimoto atauyatsa ulendo-tu apa.
07/08/2026

Eish! Apule Chikomeni awambwandira Ali ndi Zaza mgalimoto atauyatsa ulendo-tu apa.

Eish komatu zili kuno! πŸ™Œ
31/07/2026

Eish komatu zili kuno! πŸ™Œ

Mkulu uyu Saint ali ndi vuto loti nyimbo sachita kutulutsa ngati mwa kale muja which makes him not that much relevant. M...
30/07/2026

Mkulu uyu Saint ali ndi vuto loti nyimbo sachita kutulutsa ngati mwa kale muja which makes him not that much relevant. Malo ake alipo mmakutu a anthu but the silence imawonjeza mpaka pena anthu amadzaiwalako zoti kuli iyeyo.

Music ya pano ndi yokanganirana, oimba adachuluka pano so amene wabebetsayo anthu akumatsata kwambiri emweyo.

Saint has to make sure he's back mokhazikika bwinobwino, otherwise kungoimbiratu zingapo nkumangotulutsa apo ndi apo.

Unless ngati Pali mapulani enatu mwina.

30/07/2026

Ukwati watheka basi!

Your favorite female rapper, Morale. πŸ™‚β€β†”οΈ
30/07/2026

Your favorite female rapper, Morale. πŸ™‚β€β†”οΈ

Koma zingakhale zoona zikumvekazi?
30/07/2026

Koma zingakhale zoona zikumvekazi?

28/07/2026

Ahh Ahh yatulukanso ina?

🫩

Eish.. mtengo wanji uwu? 🫩
28/07/2026

Eish.. mtengo wanji uwu? 🫩

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pamtondo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share