BUNDA EYE

BUNDA EYE Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from BUNDA EYE, Box 219, Bunda, Lilongwe.

BUNDA EYE is a media platform developed by Bunda Communication and Journalism students under the Department of Agricultural Education and Development Communication at LUANAR.

25/09/2026

SPORTS
2027 QUALIFIERS-BINGU STADIUM

FULL-TIME

MALAWI 2-1 SOUTH SUDAN

MAXIMUM POINTS SECURED🔥🔥🔥

25/09/2026

SPORTS
2027 QUALIFIERS-BINGU STADIUM

GOOOOOOOOAL - LlOYD NJALIWA HAS SCORED FOR MALAWI

MALAWI 2-1 SOUTH SUDAN

🔥🔥🔥

25/09/2026

SPORTS
2027 QUALIFIERS-BINGU STADIUM

SECOND HALF IS UNDERWAY AND SUDAN HAS EQUALISED

MALAWI 1-1 SOUTH SUDAN

GAME ON🔥🔥🔥

25/09/2026

SPORTS
2027 QUALIFIERS-BINGU STADIUM

HALT- TIME

MALAWI 1-0 SOUTH SUDAN

   umu ndimmene timu ya fuko lino iyambire madzulo ano pamene ikusewera ndi south sudan pa Bingu stadium...
25/09/2026



umu ndimmene timu ya fuko lino iyambire madzulo ano pamene ikusewera ndi south sudan pa Bingu stadium...

25/09/2026

SPORTS
# FRIENDLY MATCH -CHILOWA GROUND

Full time

LUANAR MITUNDU BAPTIST 4:0 LUANAR FC

🔥AKHAPIRANA KWAKUTHWA🔥

25/09/2026

SPORTS
# FRIENDLY MATCH -CHILOWA GROUND

Second half

LUANAR MITUNDU BAPTIST 4:0 LUANAR FC

  GAWO LINA LA MGWIRIZANO WOSAYINIRA  NGONGOLE YA BOMA KWA OPHUNZIRA APA BUNDA LIKUPITILIRAGawo  la ndondomeko  yotchedw...
25/09/2026




GAWO LINA LA MGWIRIZANO WOSAYINIRA NGONGOLE YA BOMA KWA OPHUNZIRA APA BUNDA LIKUPITILIRA

Gawo la ndondomeko yotchedwa bonding potsimikiza kutenga ngongole ya boma ikupitilira kwa ophunzira apasukulu ya Bunda campus.

Ophunzira ena adandaula ndi momwe ndondomekoyi ikuyendera ku malo omwe Bungwe lopereka ngongoleyi likupitiriza kusayinitsa mgwirizanowu.

Izi zawoneka pamene kumaloku kukukhala chinamtindi cha anthu pa nthawi imodzi komanso chimpwirikiti popeza aliyese akufuna athandizike mwachangu.

Mmodzi mwa ophunzira pasukuluyi yemwe ndi Allan James wati ndondomekoyi sikuyenda bwino chifukwa bungwe la Bunda Student Union(BSU) silinatsate dongosolo loyenera monga momwe Iwo adafotokozera pachiyambi mmene zidzakhalire.

" Tili odabwa kuwona ophunzira a class iliyonse akungofika kumaloku mosatsata dongosolo limene a BSU adafotokozera pachiyambi ndipo ndizachisoni kuti ophunzira ochuluka akulawirira mmawa kwambiri kuthamangira kumaloku ndikumakalimbananso pa nzere kufuna kupeza thandizo mwachangu", Iye anayankhula motero.

Allan wati nkofunika kuti a BSU apeze njira ina yowonetsetsa kuti ntchitoyi iyende mwadongosolo loyenera.

Wachiwiri wa pampando wa pulesidenti pa sukuluyi, Chawanangwa Malongo wati Vutoli ladza kaamba ka kusintha kwa tsiku limene ntchitoyi imafunika iyambile.

"Ngakhale pali kusinthaku, ophunzira ayenera kukhala ovetsetsa ndi oleza mtima pa nthawi imene ntchitoyi ili mkati chifukwa chilichose chikuyenda bwinobwino popanda mavuto aliwonse," iye watero.

Malongo wati iye pamodzi ndi bungwe lawo awonetsetsa kuti chilichonse chiyende mchimake ndikuti ophunzira aliyense athandizike moyenera podzafika tsiku lotsiriza chifukwa ngakhale chitetezo chawo nchokwanira.

( Olemba: Andrew Jaziel / 25/09/2026)

  LUANAR STUDENT NAMED FINALIST AT TICON AFRICA EXCELLENCE AWARDS A third year Food and Nutrition Science student at the...
25/09/2026




LUANAR STUDENT NAMED FINALIST AT TICON AFRICA EXCELLENCE AWARDS

A third year Food and Nutrition Science student at the Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (LUANAR), Aubrey Kachinjika, has been recognised as a finalist at the TICON Africa Excellence Awards 2026 in Livingstone, Zambia, for his E-Flood Innovation.

Speaking with BUNDA EYE, Kachinjika said the recognition is an honour and opportunity to represent Malawi and LUANAR on a continental stage.

"Although I was unable to attend the conference physically due to challenges in mobilising sufficient funds in time, the recognition remains a significant milestone for the Innovation and it's potential to contribute to disaster preparedness across Malawi and later the whole Africa" he added.

Kachinjika has previously represented Malawi in various technology and innovation programmes and is the Founder and CEO of Resilient Africa Technologies Limited, through which he is developing technology based solutions aimed at improving early warning systems, help vulnerable communities prepare for floods and lightning related disasters and strengthening disaster resilience.

Kachinjika is also a Youth Envoy of Malawi under ITU-Generation Connect Youth Envoys Program (2026-2030) in Switzerland.

(Reported by Chimwemwe Kawonga Kasonda 25/09/2026)

LUANAR MITUNDU FC will play against LUANAR MITUNDU RESERVE this afternoon at Chilowa ground at 2:30.
25/09/2026

LUANAR MITUNDU FC will play against LUANAR MITUNDU RESERVE this afternoon at Chilowa ground at 2:30.

Address

Box 219, Bunda
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BUNDA EYE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share