URBAN MUSIC PROMO

URBAN MUSIC PROMO MALAWI ENTERTAINMENT PAGE🇲🇼! Boost your music career and business with us!
(19)

For music promotions, contact us on 0992531112 / 0981090745

Follow us on channel👉https://whatsapp.com/channel/0029Vb65v89CXC3C6a34Q51J

20/06/2026

Zosezi ndi amuna A Dorothy 🔥

20/06/2026

Apa zimakhala kuti Scammer wakumana nazo😅

Big congratulations to Gwamba  on becoming the new Brand Ambassador for Nyasa Big Bullets! 🔥🇲🇼
19/06/2026

Big congratulations to Gwamba on becoming the new Brand Ambassador for Nyasa Big Bullets! 🔥🇲🇼

 madness "Ndachimina" hit maker🚨
18/06/2026

madness "Ndachimina" hit maker🚨

18/06/2026

Gwamba u Goat 🐐 anauyamba ndi kale 🔥🚨

18/06/2026

Shano index ndi Dolo kwambiri 🔥🔥
Chaka chino kulibe kupuma🚨

nthawi Ina ku zodiak Tv kunali mkulu uyu amabebesa🚨
18/06/2026

nthawi Ina ku zodiak Tv kunali mkulu uyu amabebesa🚨

18/06/2026

Hip-hop IKK watero uku👇

Mkazi Uyu Ndathesa Chibwezi Chifukwa Ndi Wa Ku South Africa 🇿🇦,
Ndimayenera Kupita Ku Holiday Ku SA Ndasitha Ticket Ndipita Dziko Lina Ndapanga Izi Pokumva Chisoni Ndi Abale Anga Komanso Anzanga Omwe Akuvutika Ku SA🇿🇦..
Nokha Mwamuona Mfumu Ya Nyau Ikubweresa Mkazi Waku SA 🇿🇦 Kuno Ku Malawi 🇲🇼 Dzana Dzanali Ndikamati Ndi Munthu Opanda Umuthu Mwaonatu 🤷🏽‍♂️
Ma Sponsors Nawo Mkumapanga Sponsor Birthday Zopusa Ngati Zimenezo

‼️⚠️‼️. with Malawians.

Apa timati Mbuzi yakumana ndi Mbuzi izake 🔥🔥Temwa Chawinga & Messi⚽
18/06/2026

Apa timati Mbuzi yakumana ndi Mbuzi izake 🔥🔥
Temwa Chawinga & Messi⚽

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when URBAN MUSIC PROMO posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to URBAN MUSIC PROMO:

Share