Clemes Envee

Website

Clemes Envee ARTIST || SINGER || SONGWRITER

Music is my voice, passion is my story. Creating music to inspire, unite and touch lives.

VOCAL RIDER PRESENT ( volume/level control )

THE VOCAL RIDER PRESENT ( volume/level control )👑
07/09/2026

THE VOCAL RIDER PRESENT ( volume/level control )👑

Osadandaula ma fans anga ❤️ Zonse zikhala bwino. Ngakhale nthawi zina zinthu sizikuyenda mmene timafunira, tisataye mtim...
05/09/2026

Osadandaula ma fans anga ❤️ Zonse zikhala bwino. Ngakhale nthawi zina zinthu sizikuyenda mmene timafunira, tisataye mtima. Mulungu ali nafe ndipo nthawi yake ndi yabwino nthawi zonse. 🙏❤️

Zikomo kwambiri chifukwa cha chikondi chanu, support yanu komanso kupitiriza kukhala nane pa ulendowu. Mulungu akudalitseni nonse kwambiri. ❤️🙏🎶

“Ngati Yehovah Mulungu akupitilizabe kutisunga ndi moyo, ndiye kuti akadali ndi cholinga pa moyo wathu. Mpaka pano, ulen...
03/09/2026

“Ngati Yehovah Mulungu akupitilizabe kutisunga ndi moyo, ndiye kuti akadali ndi cholinga pa moyo wathu. Mpaka pano, ulendo wathu sunathe. Tiyeni tipitirize kumukhulupirira, chifukwa nthawi yake ikadali m’manja mwake.” 🙏❤️

Amatipatsa nthawi yochuluka patsiku komanso pa sabata, moti kutengako nthawi yochepa kugwada ndi kumutamanda Mulungu sikungalepheretse zolinga zathu. 🙏

Tiyeni tizisonyeza kuyamikira kwathu pomupembedza ndi mtima wonse, mu mtendere komanso ngakhale tikukumana ndi mavuto. ❤️

Ngati Yehovah akupitilizabe kutisunga ndi moyo, ndiye kuti akadali ndi cholinga pa moyo wathu. Tisaiwale kumuthokoza pa chilichonse. 🙏❤️

Clemes Envee📌
01/09/2026

Clemes Envee📌

"Hivi karibuni nitakuja na nyimbo ya audio na video, basi naomba support yenu tafadhali."💔
26/08/2026

"Hivi karibuni nitakuja na nyimbo ya audio na video, basi naomba support yenu tafadhali."💔

These are the Madyedwe Side. At that time, they were based in Gologota Area 23, where they used to perform really good D...
19/08/2026

These are the Madyedwe Side. At that time, they were based in Gologota Area 23, where they used to perform really good Dancehall music. You can visit their page and see for yourself.🤣🔥

🔥📌
17/08/2026

🔥📌

15/08/2026

Nyimboyi taiveleni nde mundiyakhule

15/08/2026

Ndinu akuti tiziwane,
Ndikakhara ine ndiwaku Lilongwe.😊

12/08/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Alfredol Danialloh Ghausi, Zachariah Elder Chinong'one, Wesly Chilumpha, Pacharoh Thomas, Mack Hussen, Greshan Mtemera, Chester Ephraim, Isaac John, Vidah Kay MW, Damijacs Andrea, Francis Bestar, Naomi Mkandawile, Chinsis Chapora, Flossy Chawawa, Benard Macherero, Frank Chitsanzo, Enock Katolonje, Inoss Ferro, Felix Singano, Benfod M Chimkwende, Albelito Isaac, Raymond Exton Livayo, Espar Beibs, Muzikumbukila Tsiku la Yehova, Harvey Makhumula, Dalitso Bwanali, Milika Chefie, Magret Bonongwe, Raphinha G Lifitone, Kondwan Saini Diness, Maki Hatoni, Tiyanjane Banda, Lukherē Wøñgie, Bholly Chaola, Debrah Bandah, Masauko Thomas, Gift M'khutumwagalu, Ronex Rossi, Mallah Manyoni, Mercy Mughogho, Liston Malunga, Tonny Khamfula, Njala Pempho, Wa Oda Sellah, Mustapher Inosentiy, Seli Mndau, Yamuzy Hoseya, Raner Meanj, Razarous Banda, Role Modell Vikheh

Address

Area 22
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Clemes Envee posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category