Mlakatuli Ericko Mustapher

Mlakatuli Ericko Mustapher Malawian poet who recites spiritual and cultural poems, he hails from DOWA district TA MSAKAMBEWA , MOYA Village, he is also a Silver strickers fan .

Mabankers coach ndiyemweyu sitikusintha, coach odekha opanda phuma popsnga ziganizoπŸŽ‰Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰  ndi nzeru πŸ’ͺ
18/08/2026

Mabankers coach ndiyemweyu sitikusintha, coach odekha opanda phuma popsnga ziganizoπŸŽ‰

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Mabankers monga mukudziwa kuti team ya silver strikers ladies ikhale ikupita mdziko la Botswana kukatenga nawo gawo mu m...
18/08/2026

Mabankers monga mukudziwa kuti team ya silver strikers ladies ikhale ikupita mdziko la Botswana kukatenga nawo gawo mu mpikisano wa COSAFA omwe uchitike mwezi uno kuyambira pa 19 mpaka pa 30 August, mphuzitsi wa team ya silver strikers ya mpira wamiyendo koma osewera ake atsikana Andrew Chikhosi watulutsa mndanda wa atsikana omwe akatumikire teamyi ku mpikisanowu monga mukuonera mchithuzichi, team inyamuka mawa pa kamuzu international airport kupita ku Gaborone, tiyeni tifunire zabwino zonse atsikana athu πŸ₯³

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Mabankers mukuona koma zinthu zake et?, Angerezi oyimbira mpaka kumugwira mkhosi kumamunong'oneza anvere pamene paja una...
18/08/2026

Mabankers mukuona koma zinthu zake et?, Angerezi oyimbira mpaka kumugwira mkhosi kumamunong'oneza anvere pamene paja unachita bwino kuyimba offside tikadaluza πŸ˜‚πŸ˜‚πŸŽ‰

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

18/08/2026

Akazi ambiri ndabwinobwino timawasokoneza ndamunafe πŸ˜‚

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Mabankers lero ku page ya sapota wa Ekhaya Levitiko mmmm kwachuluka ma post amilandu kuluza sizinthu πŸ˜‚πŸ˜‚, komatu mukafuna...
18/08/2026

Mabankers lero ku page ya sapota wa Ekhaya Levitiko mmmm kwachuluka ma post amilandu kuluza sizinthu πŸ˜‚πŸ˜‚, komatu mukafuna ma jersey munthu amene angakuthandizeni pokugulitsani Jesery komaso kukutumizirani komwe mukukhsla ndi Iyeyu πŸŽ‰

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Mabankers team ikamachita bwino timanva kukoma kuma stand 😊, madam Edith Kachigunda wezulo pakamwa apopo nyimbo yomwe im...
18/08/2026

Mabankers team ikamachita bwino timanva kukoma kuma stand 😊, madam Edith Kachigunda wezulo pakamwa apopo nyimbo yomwe imayimbidwa ndi yoti chaa?πŸ˜‚ πŸŽ‰

Mabankers Komatu bullets ndi Ekhaya umayaka, awaawa adzaphana tsiku lina , Angerezi onani mzanuyo chonchi angapambane nd...
18/08/2026

Mabankers Komatu bullets ndi Ekhaya umayaka, awaawa adzaphana tsiku lina , Angerezi onani mzanuyo chonchi angapambane ndi Ekhaya?πŸ˜‚

Team ndi πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Mabankers Sunday likubwerali silver Strikers vs Dedza Dynamos mu fdh premiership pa silver stadium πŸŽ‰Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰...
18/08/2026

Mabankers Sunday likubwerali silver Strikers vs Dedza Dynamos mu fdh premiership pa silver stadium πŸŽ‰

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Mabankers mmakwana kwambiri madam Edith Kachigunda banker wankulu, ngati iweyo ndi fan wabankers nde sudandipange follow...
18/08/2026

Mabankers mmakwana kwambiri madam Edith Kachigunda banker wankulu, ngati iweyo ndi fan wabankers nde sudandipange follow udzifuse wekha kuti silver strikers yomwe umasapotayo ndi itiyo?πŸ˜‚

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Angerezi tationetseni achitetezo anuwo ife athu mabankers ndamenewa, achitetezo osamba πŸŽ‰Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰  ndi nzeru ...
18/08/2026

Angerezi tationetseni achitetezo anuwo ife athu mabankers ndamenewa, achitetezo osamba πŸŽ‰

Team ndi bankers πŸ₯³πŸ’™πŸŽ‰
ndi nzeru πŸ’ͺ

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mlakatuli Ericko Mustapher posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category