Amunah Achisale

Amunah Achisale 👉Freshlenz Studio Photographer 📸
👉〽️IKOZI NETWORK 📸 📹
👉Event's ..Photographer°📸
👉Mult-Award-Winning Photographer📸 🏆🏆🏆
👉International-Photographer 📸
(5)

Nde kunali Joyce Meyer mafana ambiri amkadana nayenso ngat Mateyu uja😹😹😹😹Nthawi// mwamkumbukira?Joyce Meyer ministries 👏
23/08/2026

Nde kunali Joyce Meyer mafana ambiri amkadana nayenso ngat Mateyu uja😹😹😹😹

Nthawi// mwamkumbukira?

Joyce Meyer ministries 👏

Kodi mwati chinachitika ndichani mu chaka cha 1582 date inachoka pa 4th Thursday mawa lake mkudzafikila pa 15 Friday. Ta...
23/08/2026

Kodi mwati chinachitika ndichani mu chaka cha 1582 date inachoka pa 4th Thursday mawa lake mkudzafikila pa 15 Friday. Taonani calendar yanuyo apa panadyedwa ma next anji Kaya Remote linali ndindani?🙆‍♂️

Iwe amene umkayidya History kugeri tiuze😹

Pasitara uyu mafana ambiri ankati akathabwadya TV 📺 yakwao chakumadzulo tym imeneyo kuli TVM ankayizimitsa kudikla amali...
22/08/2026

Pasitara uyu mafana ambiri ankati akathabwadya TV 📺 yakwao chakumadzulo tym imeneyo kuli TVM ankayizimitsa kudikla amalize kaye service yake.😂😂 mafana ambiri anamuyiwala 😂komanso mafana ambiri mukamika panja kumuwida😹😹

TV 📺 yakenso ya Black & white tachoka kutali😹😹

Mphake nde sitayilo lake la mmutu😂👏

22/08/2026

China 🇨🇳 ilibe tulo ndipo anthu awawa samagona tekinolojeeee iwowa afika nayo pa mponda Chimera 🙌🙌🙌 usiku wathawu ndipo ndinadhabhako zochepa video yache ili mmusimu ndipo Malawi yadziwanso yanzako ikadzuka kumachemelera inu aaaah ma Drone fafafandede (500) akamauluka onse pamodzi mkumatchaya mapikitcha anga kanema ulemu wanu a Chinese Embassy in Malawi mwationetsa zabwino🤝 🙌🙌👏👏

Pamakina 📹

Eeeeeh ma china 🇨🇳 anabwera 🔥🔥🔥🙌🙌 koma yah awawa kwao samagona amakhala busy. Ndipo drown show yayenda bwino ndipo tawad...
21/08/2026

Eeeeeh ma china 🇨🇳 anabwera 🔥🔥🔥🙌🙌 koma yah awawa kwao samagona amakhala busy. Ndipo drown show yayenda bwino ndipo tawadhabha Chinese Embassy in Malawi yadziwa kulakwa Malawi inatuluka ndipo Tekinorojeeeeeeee ili ku china 🇨🇳 ulemu wanu🔥🔥🔥🙌🙌

Ghetto yakondwera koopyaaa🔥🔥🔥

Pamakina 📸

Tikudhabha😂🔥🔥
21/08/2026

Tikudhabha😂🔥🔥

Zikufuna ziziyambika ku BICC. Usiku uno kuli Drone show

[ 📸 Amuna Achisale ]

Yakonza izi ndi Chinese Embassy in Malawi

Lero kucheme usiku uno ndiku Bicc komwe kukhale kuwulutsa ma drone fafandede pakamodzi🙌🙌🙌🔥🔥Amuna Achisale nawonso akakha...
21/08/2026

Lero kucheme usiku uno ndiku Bicc komwe kukhale kuwulutsa ma drone fafandede pakamodzi🙌🙌🙌🔥🔥

Amuna Achisale nawonso akakhala ali konko pamakina 📸kudhabha oho mpaka ma drone amenewo adziwe kulakwa kwao🤣🤣

Zabwino zippnse apa? Zonsezi akunga ndi a Chinese Embassy in Malawi 🇲🇼

19/08/2026

Iyiyitu straight ndi pweteketsa yopita kwama boys a Flames 🤣🤣

19/08/2026

Oyeneradi kuwakweradi ndazimayidi omwewadi (Scorchersdi)🤝

Chadya 1 ku National youth Summit 2026 ku Bicc ndipo chafotokoza bwino lomwe zaulendo wamaphunziro ake momwe anachitira ...
18/08/2026

Chadya 1 ku National youth Summit 2026 ku Bicc ndipo chafotokoza bwino lomwe zaulendo wamaphunziro ake momwe anachitira anakumana nazo zokhoma koma iye sanafooke .eeeeeh !! Ndipo akufuna kudzakwanilitsa khumbo lake lodzakhala Dotolo oyamba mudera lakwawo.🙌🙌🙌

All the Best Duwama👏

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Amunah Achisale posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share