Dj kenzo page

Dj kenzo page Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Dj kenzo page, Lilongwe.

04/11/2025

😂😂😂😂 gwiii means mbwandi.
Ndakusowatu phwanga.

04/11/2025

Lelo tiyambakaye ndika small ampifire ndipo yeselan mawa ndikubwera ndi yayikulu 2000w osayiwala kupanga follow page iyi 👉 Dj kenzo page

04/11/2025

Dolo kwambiri Zeze ndipo uyuyu ndiwakewa Dorothy Kingston - Cashie Madam osamakhar ndi nsanje

Ambiri Akufusa kt Kodi Dj kenzo zida zakozi amakukhomera ndindan? Ndati ndiyankhe fuso lanupa page pano amandikhomera nd...
04/11/2025

Ambiri Akufusa kt Kodi Dj kenzo zida zakozi amakukhomera ndindan? Ndati ndiyankhe fuso lanupa page pano amandikhomera ndi kaswiri uyu Dj smoko ndidolo kwambiri zosezi nda poster anakhoma ndi iyeyu kwa amene mwafilaso kuti munthuyi ndi dolo number yake ndi iyi 0999792075 osayiwala kupangaso follow page iyi 👉 Dj kenzo page ngati simunapange zikomo

lelo madzulo ano tiphuzitsana izi 👇 pangan follow Dj kenzo page  kuti tidziyendera limodz zikomo 🔥
04/11/2025

lelo madzulo ano tiphuzitsana izi 👇 pangan follow Dj kenzo page kuti tidziyendera limodz zikomo 🔥

04/11/2025

😩😩😩 iwe Onesimus Muzik ndikufuna ndlama zanga ndinapeza watcholamo crossover 😂😂

ah apatu nde ndili nfanadi et 😂😂
03/11/2025

ah apatu nde ndili nfanadi et 😂😂

Anthu Aku BT pali staff ma speaker awiri awa ma hybrid sanagwilidweko 250wts ndikufunapo 350pin BT mwayi wanu uwu imbani...
03/11/2025

Anthu Aku BT pali staff ma speaker awiri awa ma hybrid sanagwilidweko 250wts ndikufunapo 350pin BT mwayi wanu uwu imbani 0990652701 osayiwala kupanga follow page iyi 👉 Dj kenzo page

03/11/2025

Alindi mwana agwilitse 😂😂😂🙆

02/11/2025

Uthenga wa ulele uwu pangan follow Dj kenzo page lelondi timven bs 🔥🔥

31/10/2025

Azimay awawa ndathananawo onse atsara atsikana tiyambepo nchezo 🔥🔥🔥 follow this pagDj kenzo pageage

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 05:59 - 17:00
Tuesday 05:00 - 21:00
Wednesday 05:00 - 22:00
Thursday 05:00 - 21:00
Friday 05:00 - 22:00
Saturday 04:06 - 23:00
Sunday 05:00 - 22:00

Telephone

+265988118636

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dj kenzo page posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share