Mr Joke's

Mr Joke's Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mr Joke's, Art, Lilongwe.

Guys, Pali Competition yomwe ukuyenda ku TikTok, Competition yake ndiyoti Munthu ukangovina bwino nyimbo ya mfana uyu PE...
02/04/2026

Guys, Pali Competition yomwe ukuyenda ku TikTok, Competition yake ndiyoti Munthu ukangovina bwino nyimbo ya mfana uyu PEXS COLONIAL ujumakandira ndalama pompo pompo.

Number 1 50,000
Number 2 30,000
Number 3 20,000

Choncho, ngati mukufuna ka 50 pin mwachangu, Vinani nyimbo ya Pexs Colonial.

Izi zikhala zikuchitika Mpaka Mwezi wa June.

Pangani join challenge potsatira link yomwe ili mu comment section.

01/04/2026

Ndikufuna Actress yemwe tikhoza kujambula naye ma Video angapo, koma akhale wochokera ku Blantyre, chifukwa ifenso tili ku Blantyre. Koma akhale wachi Mbina kwambiri, Komanso wadongosolo muzochitika zake. Maka Wodziwa kubvala.

Ngati alipo, ayimbe pa nambala iyi.

099 66 66 7 66. ino Mr Joke's

01/04/2026

Okay, paja ndanena kuti, ndili ndi Business Idea yoti titsegule ma Company athu, achinyamata asamangokhala. Ndiye Kwa amene amadziwa ntchito za Manja, andipeze pa Whatsapp.

Call/Whatsapp: 099 66 66 7 66.

Komanso osaiwala kupanga follow page ino Mr Joke's

Today, I stand humbled and grateful… 🙏1 MILLION FOLLOWERS on Facebook. 🎉🔥This is not just a number — this is a family. A...
01/04/2026

Today, I stand humbled and grateful… 🙏

1 MILLION FOLLOWERS on Facebook. 🎉🔥

This is not just a number — this is a family. A journey. A dream that started with nothing but belief, passion, and consistency.

From the days people doubted me… to today, where a million people have chosen to follow, support, and laugh with me — I say THANK YOU. ❤️

Every like, every share, every comment… you built this. You made Mr Jokes who he is today.

To those who have been with me from day one, and to those who just joined — I appreciate you more than words can explain.

This is just the beginning. Bigger content, bigger shows, bigger impact is coming. 🚀

Let’s keep growing together!

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mr Joke's posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category