Trendtunes Malawi

Trendtunes Malawi Arts and entertainment website
For upload... 0999648453

09/02/2026

pali zambir zomwe zikuyenda pa Malawi pano... ungofunika kulimba ntima basi

“MA PRODUCERS ENA IN MALAWI ARE WORTH 1 MILLION KWACHA FEE” - EvanzMuzikHe writes:Ras,Nthawi zambiri ma artists tikapita...
08/02/2026

“MA PRODUCERS ENA IN MALAWI ARE WORTH 1 MILLION KWACHA FEE” - EvanzMuzik

He writes:

Ras,

Nthawi zambiri ma artists tikapita m'ma studio ambiri zimapezeka kuti tapanga record nyimbo yonse then 2 minutes later ma vocals akumveka ngati awamixer kale.

Basitu amakhala kuti ma producer angoyika preset ya ma plug-in oti anayuza kale pa artist winawake and zinawamvekela bwino nthawi imeneyo m'ma speaker awowo basi ati nyimbo yangotsala kuyipanga master ngati kuti amathanso mastering akunenayo.

Ma plugin ake oti angowapanga download pa ma website awulere. Ndi izi zikumapezeka nyimbo za ma artist zikufanana heavy ku Malawi.

Ndi ma producer ochepa ku Malawi omwe amafatsa ndi kuyika ma plug-in ogwirizana ndi voice ya artist yemwe wapanga record nthawi imeneyo and DJ Sley is one of them.

Pano ndi awa agundika akuti ma session aziyambila K1,000,000. To be honest, creativity, customer care and music quality yama producer ambiri ili very bad and only few producers in Malawi are worth this fee.

Nyimbo zake ziti? Izizi zoti timangotumiza beat yapa Youtube kuti mupange yofanana? Khalani serious; K1Million si ndalama yamasewera ku Malawi.

Ma studio ambiri ku Malawi ali ku chipinda za mu nyumba za makolo ama producer and salipira misonkho ku MRA kapena ma Business Premises License ku district/city council.

Basi tizingowasonkhela ma producer ndalama zomwela mowa, kugula ma airforce afake, nkupeza ma bebi m'makwalalamu basi; ambiri equipment anasiya kugula kalekale, angodalira ka soundcard ka Focusrite basi.

At this point, I encourage every artist to buy their own recording equipment. It will save you so much money.

happy birthday atate
08/02/2026

happy birthday atate

nyauyu naye amalalata eeesh a mwinza awathira fireee uku.  ATELO ali madzi
08/02/2026

nyauyu naye amalalata eeesh a mwinza awathira fireee uku. ATELO ali madzi

Madam ZE.... ati zithe
22/01/2026

Madam ZE.... ati zithe

Breaking News 😳😳❤️❤️❤️Jackie Chan has announced that he will donate all his wealth to charity. He made it clear that he ...
28/12/2025

Breaking News 😳😳❤️❤️❤️

Jackie Chan has announced that he will donate all his wealth to charity. He made it clear that he has already donated 50%.

He said his son should go out and make his own money, and if he cannot, or is not capable of doing so ,then he might just squander everything Jackie worked for.

He has already written everything into his will, stating that when he dies, all his wealth should be handed over to charity to help people around the world.

Wow, this is truly beautiful.

Moral lesson : Some next of kin end up squandering all you worked for but then still give them small.

congrats
28/12/2025

congrats

happy birthday guys... nonse ndimadolo
28/12/2025

happy birthday guys... nonse ndimadolo

28/12/2025

Good morning people
lero madzuro uno kuli bundle😎

Uthenga sulemera
28/12/2025

Uthenga sulemera

Atelo 😂😂
27/12/2025

Atelo 😂😂

Style yake ndiyomweyo bas
27/12/2025

Style yake ndiyomweyo bas

Address

Area 36
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Trendtunes Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Trendtunes Malawi:

Share