Zekho B Mw

Zekho B Mw New tech everyday

22/11/2025

Kakule SDA church

19/04/2025

Good morning

10/04/2025

Good morning fam

09/04/2025
A Polisi munzinda wa Lilongwe amanga James Gerald wazaka 18 pomuganizila kuti ndimmodzi mwa anthu omwe akhala akubela an...
13/03/2025

A Polisi munzinda wa Lilongwe amanga James Gerald wazaka 18 pomuganizila kuti ndimmodzi mwa anthu omwe akhala akubela anthu pa ABC ndi Gateway Mall.

Pa 1 February 2025 Gerald ndi anzake anaopseza ndizikwanje anthu awiri pa Gateway Mall pamene amafuna kukwela galimoto zaku 49 ndikuwabela katundu wandalama zokwana 1.3 million kwacha.

Patsikuli anthuwa anabeledwa katundu kuphatikizapo play station game, zikwama ndi ma lamya ammanja.

Khumbo Sanyiwa wachiwiri kwa mneneri wa Polisi ya Lilongwe wati Gerard ndi anzake omwe akuwasaka amagwiritsa ntchito zikwanje pobela anthu pa ABC ndi Gateway Mall.

Iye wati Gerald akhala akukaonekela Kubwalo lamilandu posachedwapa.

Address

Likuni
Lilongwe

Telephone

+265996211257

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zekho B Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Zekho B Mw:

Share

Category