Autice Mdzuma the poet

Autice Mdzuma the poet Poet and Chinese student

Boyz koma ndichilungamo ichii?? πŸ˜‚πŸ€£
29/08/2026

Boyz koma ndichilungamo ichii?? πŸ˜‚πŸ€£

28/08/2026

aliyese ali ndi m'bale wake,
wakabaza m'bale wake ndi thobwa
nanga inu m'bale wanu ndani?
πŸ˜‚

28/08/2026

FRANK MTEMERA just 3 months in Marriage,and he is gone, ukwati wa best friend, classmate wanga ku MUST, tidavina mochititsa kaso, kukondwerera kuti mzathu wapeza banja. Ndizokhudza mtima kuva kuti lero mwamuna wake wamusya, koma mawa mawa mawa, lidakhaladi la mwiniwake. RIP Frank Mtemera😭

26/08/2026

β€ŽAtati Pali 50 million Ukagone Ku Mortuary Ma Bulb Ozima Ungagone?πŸ™„πŸ’”
β€Ž

Happy birthday dear love, ndakatulo ikhale   by Raphael Stima πŸ’•πŸ˜˜πŸ’•
25/08/2026

Happy birthday dear love, ndakatulo ikhale by Raphael Stima πŸ’•πŸ˜˜πŸ’•

24/08/2026

Palmer ndiye wabwera, ana mutamanga, kwatsala mkungosintha goal keeper Sanchez ndi mphale

Chelsea the winning team πŸ‘πŸŽ‰

Tikamati Jackson wa JENTA ndi ameneyu zindoko zonse balala, ayitaneni a neba πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ
24/08/2026

Tikamati Jackson wa JENTA ndi ameneyu zindoko zonse balala, ayitaneni a neba πŸ€£πŸ€£πŸ™Œ

24/08/2026

Premier league ikuyamba lero
remote handover ceremony iliko around 8pm
Chelsea vs Fulham πŸ˜‚

24/08/2026

azibambo amanyoza mabere akugwa pagulu, chosecho amaliyamwa ngati mwana wamasiye 🀣

Tichotse nkhawa brain teaser, muli mabowo angati pa malayawo
24/08/2026

Tichotse nkhawa brain teaser, muli mabowo angati pa malayawo

Address

Lilongwe

Telephone

+265990492726

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Autice Mdzuma the poet posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Autice Mdzuma the poet:

Shortcuts

Share