JM. Mishoni

JM. Mishoni welcome to JM. Mishoni. funny, story and music found it οΏ½.

Anthu a ku Burkina Faso ayamba kumutchula Ibrahim Traore kuti President wamuyayaπŸ™ŒπŸ»Izi zikuza pamene azungu amafuna alowe...
05/04/2026

Anthu a ku Burkina Faso ayamba kumutchula Ibrahim Traore kuti President wamuyayaπŸ™ŒπŸ»

Izi zikuza pamene azungu amafuna alowere pa ganizo lomwe Ibrahim Traore wayankhura lokhunza kuipa kwa Democracy

Azunguwo anayamba kutuma anthu ena a mu mdziko la Burkina Faso kuti achititse ma Demo akusakondwa pa zimene anayankhura President Traore kuti athetsa ulamuliro wa Democracy mdzikomo

Koma anthu aku Burkina Faso awauza azunguwo live live kuti β€œLeave us alone ife sitikuonapo Vuto tikazaona vuto mwina tizakuuzani koma padakalipano tili pambuyo pa President wathu Traore chifukwa chilichonse pano chikuyenda bwino ndiye musatuze zochita”

02/04/2026

game over

02/04/2026

nobiya high school

𝗠π—ͺ𝗔π—ͺπ—œπ—‘π—”π—žπ—’ π—žπ—”π—‘π—šπ—”π—§π—œ π—–π—›π—œ πŸ­πŸ¬π—šπ—• 𝗣𝗔 π— π—¬π—”π—œπ—₯π—§π—˜π—Ÿ 𝗔𝗣𝗣!?πŸ”₯π—Ÿπ—˜π—₯𝗒 π—Ÿπ—œπ—§π—›π—” π—žπ—¨π—žπ—›π—”π—Ÿπ—” π—Ÿπ—”π—‘π—¨!πŸ”₯Gulani mayunitsi kapena bandulo ina iliyonse pa My...
02/04/2026

𝗠π—ͺ𝗔π—ͺπ—œπ—‘π—”π—žπ—’ π—žπ—”π—‘π—šπ—”π—§π—œ π—–π—›π—œ πŸ­πŸ¬π—šπ—• 𝗣𝗔 π— π—¬π—”π—œπ—₯π—§π—˜π—Ÿ 𝗔𝗣𝗣!?

πŸ”₯π—Ÿπ—˜π—₯𝗒 π—Ÿπ—œπ—§π—›π—” π—žπ—¨π—žπ—›π—”π—Ÿπ—” π—Ÿπ—”π—‘π—¨!πŸ”₯

Gulani mayunitsi kapena bandulo ina iliyonse pa MyAirtel App ndikupeza mwayi ophula CHI 10GB or 100GB pa Wheel of Fortune!

Gwiritsani MyAirtel App ndikuyesa mwayi lero. Ngati mulibe pangani download wanu apa:

click here https://refer.airtel.africa/MW/UX3V8F72 and download the MyAirtel App using this code: UX3V8F72

Address

Karonga
Lilongwe
JACK1145

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when JM. Mishoni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category