Pakwathu

Pakwathu We promote Art and we storytellers .. educating the youths and encouraging them it's first priority

Pure talent sizokakamiza Nakupenda by  ft yunus
13/02/2026

Pure talent sizokakamiza Nakupenda by ft yunus

Blaze x Yunus Nakupenda Official video

Malinga posted that and Sangie  ndikudzangopanga ka comment ndi ka pic akaka koma ya Sangie amatha zithu tisanamepo mmmm...
17/11/2025

Malinga posted that and Sangie ndikudzangopanga ka comment ndi ka pic akaka

koma ya Sangie amatha zithu tisanamepo mmmmmmm .. mpake Malinga kupenga naye mmmmm sizoona

07/10/2025

Kwachaaa mupalamuleso atsikana ndi azimai paja simumvaa

Good morning

zeze 7.9 million kwacha agulila fon Dorothy  eeiish anthu ndalama muzitenga kuti ?? nde China uchimva nane ndufuna undig...
06/10/2025

zeze 7.9 million kwacha agulila fon Dorothy eeiish anthu ndalama muzitenga kuti ??

nde China uchimva nane ndufuna undigulele iPhone 17 mutu uli gwaaa or manyazi osachigwila

uyutu ndi ndalama za Cosoma izi iiiii

Or kumamwa ndikasakhabe kukhala mMalawi ine
06/10/2025

Or kumamwa ndikasakhabe kukhala m
Malawi ine

koma akudya chakwera aliko??? please Check on him kwachematu kwachema uku
18/09/2025

koma akudya chakwera aliko???

please Check on him kwachematu kwachema uku

10/08/2025

Koma or Chochokela ku malawi kuno sindimachiwona eee ....

Adhaawawa akuti anakumana ndi adha awawa nde adha awawa chani chini kaya kwinako muvela nokha 😄

10/08/2025

MADAM Kelly Kay nde akwiyilatu simmene kulili akati ndikupeza uwona ndikupeza heheee kwanukhilatu ....

hello Mr Yesu

adzibwelani basi dziko latitopetsa ili mudzatiweluze zochitika zachuluka iiiii

apa pokha palowa Tipex nyimbo zake ziti aaaaaa... ...
02/08/2025

apa pokha palowa Tipex nyimbo zake ziti aaaaaa... ...

Address

Kawale 2
Lilongwe Area 4
72006

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pakwathu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share