Chongololo

Chongololo Learn

18/05/2026

Hello

Nthawi ya zanyengo yachenjeza kuti for the next 24 hours kukhala mvula ya mphavu Muma dera ena mu dziko muno __Tiyeni ti...
16/02/2026

Nthawi ya zanyengo yachenjeza kuti for the next 24 hours kukhala mvula ya mphavu Muma dera ena mu dziko muno __
Tiyeni tikhale osamala komas a tchelu

Mkazi wa nzeru azikhala supportive kuthandizila mwamuna wake.Sankhani mwa nzeru malume
16/02/2026

Mkazi wa nzeru azikhala supportive kuthandizila mwamuna wake.
Sankhani mwa nzeru malume

Kodi mzimayi yu mukuti watani?
02/12/2025

Kodi mzimayi yu mukuti watani?

Kungoti ana a school fe sitinena koma umu ndimene zimakhalila semester ikamatha🙌
02/12/2025

Kungoti ana a school fe sitinena koma umu ndimene zimakhalila semester ikamatha🙌

02/12/2025

Nafeso timavuta koma sitinaotcheko school olo kuononga zinthu

Tikumvana ku chayamba ko?
Mukuziphera nokha tsogolo

02/12/2025

Kodi akakufusani kuti body count yanu ndichani mumayankha Chani?

Zimangofunika kuvomereza chomwe uli munthu,moyo nkumapita
02/12/2025

Zimangofunika kuvomereza chomwe uli munthu,moyo nkumapita

Address

Lilongwe
Lusaka

Telephone

+265981912266

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chongololo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Chongololo:

Share