DR NDABA

Call Contact the establishment

DR NDABA Home of entertainment 🌏📺📸
KASUNGU

Hit us on wap 0993836869

Komano ndi nyimbo iti mu album imeneyi imene Mukuti iyi yokha ajambule video !
06/10/2026

Komano ndi nyimbo iti mu album imeneyi imene Mukuti iyi yokha ajambule video !

For the first time in Kasungu... Onesmus is here to vibe with us🔥🔥🥳🥳🥳Tisamangozioner kutali let's go and make history ku...
06/10/2026

For the first time in Kasungu...

Onesmus is here to vibe with us🔥🔥🥳🥳🥳

Tisamangozioner kutali let's go and make history kuti Kasungu siyotsalira

31 December get your loved ones, family and many more to this amazing event

Mneneri wa boma, yemwenso ndiwolankhulira chipani cha DPP, Honourable Shadreck Namalomba, adandaula ndi zomwe akuchita M...
05/10/2026

Mneneri wa boma, yemwenso ndiwolankhulira chipani cha DPP, Honourable Shadreck Namalomba, adandaula ndi zomwe akuchita Ms newspaper akulu akulu mdziko muno ngati Zodiak Online, Times 360 Malawi, Nation Publications Limited zomapanga post news zakusowa kwa fuel.

"Aliyense akudziwa kuti fuel wavuta! Phindu lomapanga post zinthuzi zakusowa kwa fuel ndi chani?" Adandaula a Namalomba

Iyiyi nde yawawa😭😭Rest in peace coach jonnah😭😢😥 Sad news📰  from wene kasungu💔💔💔😰
05/10/2026

Iyiyi nde yawawa😭😭
Rest in peace coach jonnah😭😢😥

Sad news📰 from wene kasungu💔💔💔😰

Police ya Lumbadzi ku Dowa, yamanga Harrison Solomon  Steven wazaka 33 komanso Mphatso Gabriel wazaka 35 kamba kopezeka ...
04/10/2026

Police ya Lumbadzi ku Dowa, yamanga Harrison Solomon Steven wazaka 33 komanso Mphatso Gabriel wazaka 35 kamba kopezeka ndi zida zomwe akukayikila kuti awiriwa amafuna kukabela katundu penapake.

Azibambo awiriwa anawagwira atakwera nazo zidazo mu pickup pa roadblock yomwe a police anakhazikitsa pa junction yopita ku airport ya Kanuzu. Ndipo anawapeza ndi zikwanje (zitatu), mipeni (2), nkhwangwa (zitatu), ma bulgar bars, ma mask ndi Zina ndi zina. Kuwafunsa kuti mzachani, iwowa anati apeza ganyu yokaswa mphanje pena pake koma atawafunsa mowilikiza anayamba zibwibwi kufikila m'modzi oganizilidwa wo, Mphatso Gabriel , anadumpha mu lorry mo ndikuthawa.

A police anamuthamangitsa ndikumugwira.

Awiriwa aulura kuti zidazi amapita nazo ku Area 50 komwe amakakumana ndi ma gamba ena kuti akayambe ma mission.

03/10/2026

Ana masikini avuta ku Lilongwe 😂😂😂

Big mn SCABA あ umakwana🫣🫣

03/10/2026

Mupangeni tag Dr Namadingo aziwa kulakwa kwake😂😂😂

Umakwna broh Dr Dingo

30/09/2026

😂 😂 😂 Amen abusa

30/09/2026

Chikangoti.... Guwa athu ose kubalalika😂😂

30/09/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Peter Dah Goon, Con Mannah Whizie, Chimlamba Hatsman, Malala Kasungu, Kizmert Zaspy, Junior Ngolomera, Samu Higa, ɭɭ PánthérAɭɭ, Emanuel J Bulala Banda, KHEBOZ MW II, Applê Pïê, Tonex Alfred, Glo Mah, BÉÌB PRAÏSÉ ɭɭ, George Mkandawire, Mary Msukwa, Oyimbo Osumbo, Chamba Banda, Sg Kalambo, Paul MC Donald, Pinco Pinooh, Ismail Gavin, Na Tasha, Feli CHilolo, Favoured Nambazo, Wuod Nyahero, Fateson K-nox, Patrick Chitsulo, Swaxy Jonas Luke, Belyndah Brown, Huseni Mwachande, Crevng Ndalama, John Johnson, Witness Mtonga, David Phiri, Nicior Beib, Wa Ysoni, Graxy Boswell, Ynm K Ceezrah Montel

Address

KASUNGU
Kasungu

Telephone

+265993836869

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DR NDABA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to DR NDABA:

Shortcuts

Share