ByChance Isaac

ByChance Isaac Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from ByChance Isaac, Arts and entertainment, Kasungu.

20/03/2026
31/10/2025

Tumbuka my language πŸ™Œ πŸ™Œ πŸ™Œ

BORN CHRISS WALEMBA KUTI;πŸ‘‡Letter to Small Wife:Aise ndiwe Dolo ndiwe Shashaa, umavala bho,ndiwe Modelo wabho uli ndiluso...
07/10/2025

BORN CHRISS WALEMBA KUTI;πŸ‘‡

Letter to Small Wife:

Aise ndiwe Dolo ndiwe Shashaa, umavala bho,ndiwe Modelo wabho uli ndiluso.

Ndimakumbukila tsiku Lina lake ndimkakonda kukupatsa malangizo pafupifupi ,then zinakunyasa unayamba kumandinyoza kundipanga post kuti sasamba usamandipatse malangizo ako Awulere,choti udziwe ndichakuti sasamba amene amkakulangiza yo ndamene amakukonda komanso amakufunila mafuno abwino.Komabe zimenezo zinapita zinatha.

Nde chomwe ndingakuwuze ndichakuti mzako akakulangiza zimafunika kumamvela osamunyoza.

Pa Khani zomwe zachitikazi Kaya ndiwe Kaya siwe,komabe ukuyenela kuphunzilapo china chake.

Langizo lomwe ndingakupatse ndilokuti uzipanga zibwenzi ndi Amuna ozindikila a maturity,usamakonde kupanga zibwenzi ndi mayoh,

Next time ngati ungazagwenso muchikondi Pilizi Mamuna akazakuwuza kuti umutumizire uzithunzi uli bwamuswe usazalole Kaya azakwiye olo chibwenzi chizathe,Bola chibwenzi chithe kusiyana ndikuzayalutsidwa.Ndipo Mamuna ozindikila komanso wachikondi sangamuwuze okondedwa wake kuti amutumizire zinthunzi Ali maliseche never

Aise Munthu amene amakufunila zabwino ndi amene amakulangiza before scanda,Ine nakulangizapo usanapange scandal iliyonse,koma Pali Anthu Ena akukulangiza After scandal and scandal yako akuyitengela ngati njira yapangira promo nyimbo zawo komanso kuchulukitsa ma views,akumabwera nditimalangizo pamwamba m'musi ndikuzaponya ma link anyimbo zawo ma fake friends uziadziwa aise

Ukudziwa chani Sistez chibwenzi pena sichikhala chamuyaya chimatha and never trust a guy mpaka kumamutumizila ma pic olawula coz mukayambana olo kupsesana mitima Amuna enawa ndimbalame chifukwa chamkwiyo Amatha kupanga leak zithunzi zija Cholinga choti uyaluke.Nde kuti upewe zonsezi zimafunika kuzisungila ulemu,osazijambula zithunzi zolowula or uli mbulanda.REMEMBER Your Body is A TEMPLE OF GOD .Thupili kumalilemekeza.

Pali nthawi inayake umati ukukonza zinthu osadziwa kuti ukuwononga,pena u.mati ukupanga zomusangalatsa Munthu osadziwa

Click on the link below
28/09/2024

Click on the link below

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

Let's bet
28/09/2024

Let's bet

04/09/2024
02/08/2023

Let's go and hustle guys

πŸ’ͺπŸ’ͺπŸ’ͺ

27/07/2023

Whatever, put God first πŸ™

22/04/2023

I will get there

26/03/2023

Welcome elders

Address

Kasungu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ByChance Isaac posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share