T boy

T boy Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from T boy, Poet, Lukulu primary school Post office 71, Karonga.

07/08/2024

poem : Tayimilira iwe Donah

ndik*t tayimilira iwe Donah
Mutsachere Bomba koma uchere nkhutu k*t
undivesese za kunkhosi kwanga ndikonyowa
Tayimilira iwe
panthawi imene tinakumana panali mphepo wa kavuluvulu koma chifkwa chak*t unakuwa "tikuferanji ife pano unatero " mmm pamenepo
mphepo inankhala bata
pamenepo mphepo imachita kuvomeleza chilengedwe chako achemwali
Tayimilira

Ndik*t tayimilira iwe Donah
ukamandiyona dzunguli dzunguli mpakwanu ngati khunda sichina ayi!! koma ndikulempera kugona chifukwa chak*t mbali inayi panthupi panga ndinaberedwa nthiti ku GENESIS nde ndkufuna ndibwerere nawo nthitiyo
tayimilira iwe

Tayimilira iwe Donah
chuluke chuluke wa njuchi unena yomwe wakuluma zonad akadzi nd maruwa koma maruwa akayombedwa ndizuwa wamafoto koma iwe ndiwe dzuwaro mmmm
chonde tayimilira iwe

Tayimilira iwe Donah
wazaza mtima mwanga ndasowa ponthawira
ndkuziwa k*t ndkankhala ndiwe ndasiya kulira
chonde ndichilitsen mabara wa mtima mwanga
ndilimbulanda ndi vekeni mmmm
kodi unalakwisa chan kwa Mulungu k*ti iwe ngero akugetsereni pasi panooo ? mamama
iwedi chisumphi anatayo nthawi polenga
Tayimilira iwe Donah

By ZYamikani Munthali
contact 0994884484
email [email protected]

07/08/2024

I welcome you all

07/08/2024

poem.... cholinga changa
cholinga changa ine
cholinga changa ine bale
mukamandiyona ine ndili jijilu jijilu ku chalichi
sichina ayi koma cholinga changa,
munditole bwino bwino chifkwa ndikuyulurilani
cholinga changa

cholinga changa
inde k*t ndifikile cholinga cho !!
ndinthund ndkuziwa munjiramo muli mikondo
pak*ti nayeso anakumana ndinkhondo
ha ha ha !!!! koma iye anapambana pachifukwa
chi ndchokwanila kundilimbisa mtima ndik*t ndalimba mtima ngat mwara wa mphwero k*t tsinditopa, tsindifoyoka, tsinditopa tsindigonja
kumpinda mayondo kwa iye k*t ineso ndikwanilise cholinga changa
cholinga changa

cholinga changa ine
cholinga changa bale
ndik*t iyeso anali ndicholinga
pochoka kumwamba Po bwera pasi pano
cholinga chake chinali k*tiyonesa njira,
kuvomeleza kunkhomeredwa patanda cholinga
Chotilimpira ngongole zanthu , anafa tsiku lachitatu ooo !! anayuka Manda mafuna k*tiyonesa k*t iye ndimwini moyo nd ifa, ndinthu cholinga chake anakwanilisa
mamama !!! ineso cholinga changa ndikwanilisa
cholinga changa

cholinga changa ine
mumandiyona ndi kulira kwinako ndkumenya mpembero ndmalilime mkat " (likoto likoto limpampa rankuzga nkhaza mande )"ndi kusalaso chakudya
tsikufuna kwanga ayi koma cholinga cho chikundikakamiza k*t nditero
cholinga changa

cholinga changa ine bale
pamphindi zochepa chabe mundibwerekeko mak*tu k*t mundivesese bwino bwino cholinga changa ndik*t cholinga changa ine
ndkufuna NDIZAVARE KOLONA WA MOYO !!!

by ZYamikani Munthali
contact: 0994884484 .
email: [email protected]

07/08/2024

Address

Lukulu Primary School Post Office 71
Karonga

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when T boy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category