Das manford banda

Das manford banda https://youtube.com/?si=2zeJwVSS4iiEcW6d

Ndikanakhala ndani kopanda inu ambuye yesu

❤❤❤
15/07/2026

❤❤❤

😍😍😍
15/07/2026

😍😍😍

12/07/2026

MAWU OTILIMBIKISA 👇
1 timoteo 6 ves 7-

7pakuti sitinatenga kanthu polowa m'dziko lapansi, ndiponso sitikhoza kupita nako kanthu pocoka pano; 8koma pokhala nazo zakudya ndizopfunda, zimenezi zitikwanire. 9Koma iwo akufuna kukhala acuma amagwa m'ciyesero ndi m'msampha, ndi m'zilakolako zambiri zopusa ndi zopweteka, zotere zonga zimiza anthu m'cionongekondi citayiko

Das manford banda

palibe tchito yabwino ina paziko lapas pano yopamba kutumikila MULUNGU phindu lomwe ungazapeze👉osaiwala kupephera musana...
11/07/2026

palibe tchito yabwino ina paziko lapas pano yopamba kutumikila MULUNGU phindu lomwe ungazapeze

👉osaiwala kupephera musana gone🙏

08/07/2026

😍

kumamuyamika MULUNGU pa zose tili nazo ndi bwino ndipo mudaliso umafikaso mo wilikiza ine ndzyamba zikomo ambuye pazose ...
02/07/2026

kumamuyamika MULUNGU pa zose tili nazo ndi bwino ndipo mudaliso umafikaso mo wilikiza ine ndzyamba zikomo ambuye pazose mwandipasa munyemgo ino🙏👇

chi team kuchoka kokapepheraa
15/06/2026

chi team kuchoka kokapepheraa

20/05/2026

ubwino wa MULUNGU ndi oti ngakhale ndili ochimwa amandikondabe koma muthu yemwe ndinamulakwila kamozi mpaka pano zaka zikupita

zikomo ambuye chifukwa cha chikondi chanu🙏

✨♥️
14/05/2026

✨♥️

Address

Mtupi Dwangwa Khotakota
Dwangwa

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Das manford banda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category