Pabwalo Comedy Series

Pabwalo Comedy Series PABWALO COMEDY SERIES 🎭
Is based on real life β€”
what is happening in our areas,
what people go through every day,
and the experiences we all understand.
(5)

We use humor to teach, advise, and open eyes,
because laughter is better when it has meaning.

05/06/2026

Munyeliwa wachesulidwa,,,,

Mpaka kumenyana ndi Nickson Pabwalo la amfumu zoona?

Tiyeni ku YouTube channel tikaonele yonse link mu comment section

05/06/2026

Koma nkulu uyuyu atakhala wabwela kwanuko mau oyamba mungamuyankhule otichani?

Nenani ChilungamoπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

05/06/2026

:
Kwa ma Fans nonse omwe muli ndi kuthekela kothandiza Pabwalo comedy series tiyankhuleni pa number iyi yomwe ndi ya Manager
#+265989427758
Mukhoza kuimba kapena Message pa whatsap,,

1: Tilengeze ma business Anu mu ma series athu thandizolo tizithandizilaso ma actors komanso actress athu

2: Ndandizo la ndlama iliyose yomwe mungakwanitse kuti izithandiza tsiku lojambula kapena transport

Koposa posa ifeyo timakunyadilani dziwani zoti anthu onse omwe amaoneka mumakanema athu amasowaso thandizo kuti ma banja awo azithandizika kuzela mu luso koma ife ndi ochepekedwa,.

Zikomo
Management

Munyeliwa Anvekeleee ............πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚
02/06/2026

Munyeliwa Anvekeleee ............

πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Pabwalo comedy Team ikufunila Asilamu onse Eid yopambana pomwe lero kuli Chisangalaro Cha ku zinga Nyama,,,,,May your pr...
28/05/2026

Pabwalo comedy Team ikufunila Asilamu onse Eid yopambana pomwe lero kuli Chisangalaro Cha ku zinga Nyama,,,,,

May your prayers be successfully answered,,,

Allahuma AmeenπŸ™

Mawu amodzi okha kwa The CEO a Pabwalo Comedy series to day?????Uyu ndi Yass-Tech Visuals πŸ“Œ Pomwe tikuyankhula mau amodz...
27/05/2026

Mawu amodzi okha kwa The CEO a Pabwalo Comedy series to day?????

Uyu ndi Yass-Tech Visuals πŸ“Œ

Pomwe tikuyankhula mau amodzi tiyeni ku YouTube basiπŸ˜…πŸ€£πŸ€£πŸ€£

https://youtu.be/nnzCxv_-F80?si=L6ckM1xLZfOJWjA-

Address

Limbe Blantyre 3
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pabwalo Comedy Series posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category