Mikozi

Mikozi Arts and Entertainment
(1209)

Divine Providence Education Center congratulates its students on achieving a 100% pass rate in the JCE! 🎉👏Located in Lil...
23/08/2026

Divine Providence Education Center congratulates its students on achieving a 100% pass rate in the JCE! 🎉👏

Located in Lilongwe Area 23, the school is now open for admissions, with spaces available from Form 1 to Form 4.

Congratulations Ana aku Divine Providence 🎉

📞 0992 476 001

DNA King
23/08/2026

DNA King

23/08/2026

Nyimbo iyi atenge ndiyake basi. 9 year old Chimwemwe T Mayuni, a student at Malingunde School for the blind is a big fan of Malawi hiphop https://youtu.be/IlQ6QZAfFsc

23/08/2026

“ Men who really love their wives don’t do DNA tests 🧬 “ - Ayamba kutelo tu Azimayi

Sim’mene kunaliri ku Nkhotakota pa St Paul grounds pamene Ibrahim Swedi amapeleka chikho mu Suwedi Cup imene adakhazikit...
23/08/2026

Sim’mene kunaliri ku Nkhotakota pa St Paul grounds pamene Ibrahim Swedi amapeleka chikho mu Suwedi Cup imene adakhazikitsa ku Nkhotakota ko 🏆

23/08/2026

Muli Speaker

Mphoto zija ndi ‘Njinga, Feteleza, Ma Sprayer, Ma Work Suit, Ma Gambusi, Ma T shirt’.Izi zikuchitika mu nyengo ya ‘Phwam...
23/08/2026

Mphoto zija ndi ‘Njinga, Feteleza, Ma Sprayer, Ma Work Suit, Ma Gambusi, Ma T shirt’.

Izi zikuchitika mu nyengo ya ‘Phwamwawa’ ku Seedco imene ikutha pa 30th September. Onse amene akumalizitsa kulipila Mbeu zawo ku Seedco akhala ndi mwayi onyamula mphoto zi.

Mbeu za Seedco zitha kugulidwa direct ku shop iliyonse ya Seedco, Bank Transfer (Via official Seed Co bank accounts) kapena through USSD ( Dial *2027 # )



[ For further help and agronomy advice: Call SeedCo direct Toll-Free line: 2027 ]

23/08/2026

Ati Abusawo adayikila ziwanda nyimbo kuti zivine kenako zituluke. Koma abale 🤦🏾‍♂️ Nde zazepuladitu

Mu nyengo  ya ma Benz, Atsitsa mtengo opangila hire Benz kuchoka pa K275,000 kufika K149,000 pa tsiku ku Ken Tours & Car...
23/08/2026

Mu nyengo ya ma Benz, Atsitsa mtengo opangila hire Benz kuchoka pa K275,000 kufika K149,000 pa tsiku ku Ken Tours & Car hire. Izi zichitika kuyambila lero mpaka pa 30 September 2026.

Kudyela ndi wekha

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mikozi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Mikozi:

Shortcuts

Share