nzemalossi.com

Website

nzemalossi.com Entertaining you forever

I think R***r show ija sidamuwaze zoona olo kupanga post chithunzi kuti anabwera ndipo kuti tione mmene adanjanjira?anko...
02/08/2026

I think R***r
show ija sidamuwaze zoona olo kupanga post chithunzi kuti anabwera ndipo kuti tione mmene adanjanjira?
ankolo R***r bwanji koma? eeh eeh

31/07/2026

Eh koma guys
ndaona ngati malaulo olo R***r yotu sanapange post kuti watera ku page yake mmmmh mwina bundle yamuthera🤣🙌

24/06/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Saindane Ausmani, Blenda Jere Phoseka, Baba Kuna

20/06/2026

page ino ikudana ndi ma south Africans onse

we are hating all the South Africans on this page we will forever hate south Africa

Mma school mu mukhale subject yophunzitsa ana kugwira microphone tachita manyazi kutabwera alendo kwathu kuno 🙌
18/06/2026

Mma school mu mukhale subject yophunzitsa ana kugwira microphone tachita manyazi kutabwera alendo kwathu kuno 🙌

Plan yanji iyima builders polani moto eeh eeh kumanga kwabwanji ukuma builders pamudzi pano izi osazamanganso aliiiiii🙌
10/06/2026

Plan yanji iyi
ma builders polani moto
eeh eeh kumanga kwabwanji uku
ma builders pamudzi pano izi osazamanganso aliiiiii🙌

Ulimi waphindu uwu tawuyesani ndipo simuzakhumudwavuto anthu otsutsa boma makani 😂🙌
10/06/2026

Ulimi waphindu uwu
tawuyesani ndipo simuzakhumudwa
vuto anthu otsutsa boma makani 😂🙌

10/06/2026

Kupangira ana ama 2pin Inu
Iyi Ndi video ya Kamuzu yomwe adati I have come to break stupid federation
Kuthekanso kamuzu simumamudziwa
Ana amasiku ano vuto Ndi vigololo mmmmm🙌

Tikugulitsatu K1,000,000kungobaya kamozi maluzi onse kusowa mmoyo
09/06/2026

Tikugulitsatu K1,000,000
kungobaya kamozi maluzi onse kusowa mmoyo

Anzanu Ali kunja ndipo anatsekula bizimesi 🙌Mukawaona musawagulebola ndapereka langizo laulele
07/06/2026

Anzanu Ali kunja ndipo anatsekula bizimesi 🙌
Mukawaona musawagule

bola ndapereka langizo laulele

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when nzemalossi.com posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share