Wagulu Network Entertainment

Wagulu Network Entertainment Promoting Brands | Slogan | Graphic Designing | 🇲🇼

 Zimangoona kuvuta koma pena azibale anu ndi ana anu omwe mukukhala nawowo zimafunika tsiku lina kungopanga trip nkuwate...
18/05/2026



Zimangoona kuvuta koma pena azibale anu ndi ana anu omwe mukukhala nawowo zimafunika tsiku lina kungopanga trip nkuwatenga akaone moyo wa ku prison mene umakhalira mkutheka makhalidwe ena omwe amachitawo atha kusiya

Tsiku linaso kuwatenga trip ya ku chipatala ku Central, ku Queens akaone ku 3B. Khulupilirani mukamazachokera ku trip imeneko sazakhalaso Chimodzimodzi

14/05/2026



Muli inu mungatani

Mnyumba ina ya anthu olemela munalowa akuba amfuti,anatenga katundu yese ofunikila kenako apita pomwe anaima abambo ndi amayi anyumbayi

Apeleka futi kwa abambo ali ombela mkaziwako,abambo aja anayang’ana mkazi ndikupukusa mutu ataganizila chikondi conse mkaziwawo amawaonetsela,anakana ati sindingamphe mkaziwanga

Akuba apeleka futi. Kwa mkazi ali ombela mamunawako, mkazi anatenga futi uyo walozetsa mamuna wake mmutu kenako phaa

Nde futi ija inali chabe toy,basi akuba aja anangopukusa mutu ndikuseka ,kenako ndikutenga futi yawo wautali kuwasiya amayi andi abambo aja ali chiimile

Muli inu mukanatani 😃😃😃
Like and share for funny 🤣

 Madzulo abwino Kwa nonse anthu otsata Wagulu Network 🔥Lero pamudzi pano tabwera ndi nkhani ya m'nyamata uyu amene dzina...
04/05/2026



Madzulo abwino Kwa nonse anthu otsata Wagulu Network 🔥

Lero pamudzi pano tabwera ndi nkhani ya m'nyamata uyu amene dzina lake ndi Jusab 203 amene amayimba nyimbo zachikondi ndipo zomveka bwino kwambiri. M'nyamata uyu wakhala akuyimba kuchokera mu Chaka Cha 2019 kufikira pano adakapitilizabe luso lake la mayimbidwe.

Amayimba chamba Cha hip-hop komaso afro. Ndipo wayimba nyimbo zotchakuka bwino ndinso zojambulidwa bwino Ngati Manana adayimba ndi m'nyamata wina otchedwa Vertex ndipo adayimba nyimbo yotchedwa Too much imene adayimba ndi BLESS DANGER ndipo sadasiyire p***a adayimbanso nyimbo yotchedwa mpaka kale ndi Young Cidy. Jusab 203 ndi m'nyamata wolimbikira kwambiri kumbali ya luso lake lamayimbidwe.

Mukhoza kumufufuza pa ma tsamba a intaneti monga ; Audio mack, YouTube, Facebook ndi ena onse otero ndipo Jusab wauza Wagulu Network kuti akupanga zoti muzisangalala komaso kukhutira ndi luso lake lamayimbidwe.

Nyengo yamadzulowa Ili motere ; Kukuzizira pakati pa 15 ndi 20 degrees. Usiku wabwino.

  Masana anu alibwanji kulikonse komwe muli? Nyengo yatsiku lalero Pa 3 May 2026 ili motere : Dzuwa likuwara mwapatalipa...
03/05/2026



Masana anu alibwanji kulikonse komwe muli? Nyengo yatsiku lalero Pa 3 May 2026 ili motere : Dzuwa likuwara mwapatalipatali kukuzizira komanso kukutentha.

Nkhani yomwe tabwera nayo masana ano ndi ya Cosmos Thera. Amene akudziwika ndi dzina loti Director Costey mkuluyu amajambula ma Video Ndipo wajambula nyimbo, ma ukwati, zithunzi ndi zina za anthu odziwika m'dziko muno. Costey ndi munthu amene ayika chidwi akafuna kuphunzira chinthu. Kuchoka mu chaka cha 2025 chimene chili chaka chatha wakhala akuyika chidwi chake chonse pa zojambula.

Kupatula ma video, Mkuluyu ndi katakwe pa nkhani ya audio production Ndipo wakhala apanga mikisi ma kwaya komanso nyimbo za achinyamata zomveka bwino.

Costey amakhala ku Blantyre pa nthawi yomwe amapanga za audio production kufikira nthawi yomwe amaphunzira zo jambura ma video. Mu chaka cha 2025 chomwecho adapita ku mzuzu komwe ndi kumudzi kwawo. Atangopita ku mzuzu ndipamene adayamba kumupatsa ulemu pa ntchito yake yojambula. Ndipo Costey wauza Wagulu Network TV kuti safooka kufikira anthu atamudziwa ngati mene anawadziwira ojambula ngati : Seany Films, Director Tonney, Kante ndi ena ambiri.

Pangani follow page ino kuti zambiri zisakuphonyeni🔥🙌

 Oyimba amene ndi osadziwika bwinobwino mu dera lakwawo amene dzina lake ndi Bless Danger Niyabinggy komanso amatchulidw...
03/05/2026



Oyimba amene ndi osadziwika bwinobwino mu dera lakwawo amene dzina lake ndi Bless Danger Niyabinggy komanso amatchulidwa dzina loti KIN Danger. Dzina la KIN Danger linabwera kamba koti mkuluyu ndi Graphic Designer. Ndipo wagwira ntchito yake ya designing kwa zaka ziwiri tsopano. Wapangira design anthu ochuluka monga; Ababa Surgeant, Costey RedGiant, Man G, Jucer, Dadah Morer, Mary Kapenga ndi ena ambiri.

Ndipo izi zili chonchi KIN Danger wati ali pa promo yomwe watsitsa mtengo wa ntchito yake ya designing. Ndipo wanenetsa kuti Artwork ya nyimbo Olo MK1, 000 akhoza kupanga. Izi zakambidwa chonchi kamba koti mkuluyu akufuna kutulutsa EP kapena kuti chimbale cha nyimbo. Akufuna kupeza ndalama zopititsira Patali nyimbo zakezo.

Ndipo akupempha mtundu wa a Malawi umene umakhala ndi Mtima othandiza oyimba achichepere kuti, kuthekera kulikonse komwe ali nako akhoza kumupanga support Bless Danger.
Pomaliza wauza Wagulu Network TV kuti aliyense amene atamufune akhoza kumupeza mu njira izi..

Facebook : BLESS DANGER NIYABINGGY
WhatsApp : +265 (0) 889 941 444
Email @ : [email protected]

Reported by (A MA DA

Now you can find us on YouTube🇲🇼
01/05/2026

Now you can find us on YouTube🇲🇼

Promoting Brands | Slogan | Graphic Designing | 🇲🇼

Kodi Loiso dzina lake lenileni ndi ndani?Wagulu Network Entertainment
06/01/2026

Kodi Loiso dzina lake lenileni ndi ndani?
Wagulu Network Entertainment

Malawi's Short pple Waxy Kay (Kizito), JEG TELLEM (Zakeyu)😂😂😂 any way  najere atulutsa nyimbo link in comment section 🔥
06/01/2026

Malawi's Short pple Waxy Kay (Kizito), JEG TELLEM (Zakeyu)😂😂😂 any way najere atulutsa nyimbo link in comment section 🔥

Monga mukudziwira The one and only village champion ku malawi kuno🔥🔥 Giboh Pearson Phalombe Musik akukamba zoti phazi ng...
06/01/2026

Monga mukudziwira The one and only village champion ku malawi kuno🔥🔥 Giboh Pearson Phalombe Musik akukamba zoti phazi ngati vyete kaya akumunena ndani? Link🔥🚨

Ngati Vyete

Kuno ndi kumbali koma Buxy Mw ndi Dolo heavy 🔥
06/01/2026

Kuno ndi kumbali koma Buxy Mw ndi Dolo heavy 🔥

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Wagulu Network Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share