Zokambakamba

Zokambakamba Home of Local & International Sports News

FDH PREMIERSHIP RESULTS Silver Strikers 0-1 Mighty Wanderers FCEkhaya 2 - 0 Kamuzu BarracksChitipa United 2-0 Mafco FC L...
10/10/2026

FDH PREMIERSHIP RESULTS

Silver Strikers 0-1 Mighty Wanderers FC

Ekhaya 2 - 0 Kamuzu Barracks

Chitipa United 2-0 Mafco FC

LUANAR Mitundu 1-1 Red Lions

FULL TIMEMalawi 2-0 ZimbabweCongratulations Scorchers
09/10/2026

FULL TIME

Malawi 2-0 Zimbabwe

Congratulations Scorchers

08/10/2026

Brand new song from Diesel Choir

Woyimba Kell Kay akakhala akusamgalatsa anthu pomwe timu ya mpira wa miyendo ya a mayi 'Scorchers' ikhale ikukutumula ti...
08/10/2026

Woyimba Kell Kay akakhala akusamgalatsa anthu pomwe timu ya mpira wa miyendo ya a mayi 'Scorchers' ikhale ikukutumula timu ya Zimbabwe

Mawa pa Bingu National StadiumMalawi Vs Zimbabwe Go Scorchers Go! 📷
08/10/2026

Mawa pa Bingu National Stadium

Malawi Vs Zimbabwe

Go Scorchers Go!

📷

08/10/2026

Ati kumapangiratu ndithu

Malemu Atoht Manje anamwalira tsiku ngati la lero mchaka cha 2023. Ndi nyimbo iti ya Atoht Manje yomwe imakusangalatsani...
08/10/2026

Malemu Atoht Manje anamwalira tsiku ngati la lero mchaka cha 2023.
Ndi nyimbo iti ya Atoht Manje yomwe imakusangalatsani kwambiri

A Bishop Medram Chirwa a mpingo wa Fountain of Victory ku Lilongwe awamanga powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kuphedwa ...
08/10/2026

A Bishop Medram Chirwa a mpingo wa Fountain of Victory ku Lilongwe awamanga powaganizira kuti akukhudzidwa ndi kuphedwa kwa mayi Thokozani Salimu omwe amkagwira ntchito ku bank ya FDH m'boma la Dowa.

Malemu Thokozani Salimu omwe anali ndi zaka 31 anapezeka mu galimoto mwawo ataphedwa mmudzi mwa Chinkhota pafupi ndi mlatho wa Tatolonga mu nseu wa Dzaleka-Dowa.

Gulu la a Malawi omwe akukhala mdziko la United States apereka ndalama zokwana K15.9 million ku timu ya Scorchers pokond...
07/10/2026

Gulu la a Malawi omwe akukhala mdziko la United States apereka ndalama zokwana K15.9 million ku timu ya Scorchers pokondwa ndimomwe inachitira mu mpikisano wa WAFCON komanso kudzipezera malo mu mpikisano wa FIFA Women's World Cup

📷 FAM

Ngambwingambwi pa Puma ya m'mudzi😃
06/10/2026

Ngambwingambwi pa Puma ya m'mudzi😃

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zokambakamba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share