Beta Sport

Beta Sport Home of Local & International Sports News

Yapulumukira mkamwa mwa mbuzi Brazil!!FULL-TIME Brazil 1-1 Morocco
14/06/2026

Yapulumukira mkamwa mwa mbuzi Brazil!!

FULL-TIME

Brazil 1-1 Morocco



Tiyeni tibete ndi MWOS Malawi Airtel Top 8 Quarter final!Kodi Wedson Nyirenda ndi Enos Chatama wampira ndi uti?FCB Nyasa...
13/06/2026

Tiyeni tibete ndi MWOS Malawi

Airtel Top 8 Quarter final!

Kodi Wedson Nyirenda ndi Enos Chatama wampira ndi uti?

FCB Nyasa Big Bullets Vs Ekhaya FC

5 kokolo madzulo ano pa Bingu National Stadium


13/06/2026

Mizimu ikati ikukwiyire umakagwa wekhawekha pamwambo wofunikira. Wonyamula mbendera wa South Africa kugwa pamwambo wokhazikitsa World Cup ku Mexico

Katswiri wosewera mpira wa dziko la Ghana Thomas Partey amukaniza kulowa mdziko la Canada kukayimilira dziko lake ku mpi...
12/06/2026

Katswiri wosewera mpira wa dziko la Ghana Thomas Partey amukaniza kulowa mdziko la Canada kukayimilira dziko lake ku mpikisano wa World Cup.

Katswiriyu amukaniza kulowa mdzikolo ati kamba ka milandu yogwiririra yomwe akumuzenga ku London mdziko la England.

Zateromu nde' kuti katswiriyu sasewera nawo masewero a Ghana andi Panama pa 18 June.


Amukudzula TsotsiFIFA World Cup Full-time Mexico 2-0 South Africa
11/06/2026

Amukudzula Tsotsi

FIFA World Cup

Full-time

Mexico 2-0 South Africa


29-year-old Julian Quinones is the first goal scorer at the 2026 FIFA World Cup.Joni yakumana ndi Mkudzukudzu uku.
11/06/2026

29-year-old Julian Quinones is the first goal scorer at the 2026 FIFA World Cup.

Joni yakumana ndi Mkudzukudzu uku.


Icho zosekerera anthu a Xenophobia sichikupanga nawo. Chakang'antha kale.Mexico 1-0 South Africa
11/06/2026

Icho zosekerera anthu a Xenophobia sichikupanga nawo. Chakang'antha kale.

Mexico 1-0 South Africa

Basitu olo a MWOS Malawi  avomereza kuti ino si nthawi yoonera ma Indians. Remote lipite kwa munthu wa bambo awonere mpi...
11/06/2026

Basitu olo a MWOS Malawi avomereza kuti ino si nthawi yoonera ma Indians. Remote lipite kwa munthu wa bambo awonere mpira kwinaku akukunga list ya bet.

Osayiwala World Cup ikuyamba lero. Mexico ikukumana ndi South Africa.Inu mwakwera iti? Tiyeni tibete ndi MWOS Malawi  ku...
11/06/2026

Osayiwala World Cup ikuyamba lero. Mexico ikukumana ndi South Africa.
Inu mwakwera iti?
Tiyeni tibete ndi MWOS Malawi kuti tidye dzindalama .

Atakanizidwa kukayimbira masewero a World Cup ku United States of America, referee wa mdziko la Somalia Omar ARTAN wasan...
11/06/2026

Atakanizidwa kukayimbira masewero a World Cup ku United States of America, referee wa mdziko la Somalia Omar ARTAN wasankhidwa ndi UEFA kudzayimbira masewero a Super Cup pakati pa timu ya PSG ndi Aston Villa.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Beta Sport posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share