Gรชrรฃld Bรนllรค

Gรชrรฃld Bรนllรค ๐๐ž๐ฏ๐ž๐ซ ๐œ๐จ๐ฆ๐ฉ๐ฅ๐š๐ข๐ง ๐š๐›๐จ๐ฎ๐ญ ๐ฒ๐จ๐ฎ๐ซ ๐ฅ๐ข๐Ÿ๐ž ๐Ÿ’ฆ

28/10/2024

Kukwatira mkaz oyela kumaso kokha kma myendo yokuda ndimitala kale imeney ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

23/10/2024

True love is like ghost which everybody talk about and few have seen โค

23/10/2024

Uyu asamwe nawo fanta akakoza pogona. tadusa munyengo zowawa ife ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

23/10/2024

Palibe Oyimba wabwino ngat Udzudzu Ku Malawi Nyimbo olo usayikonde umawombabe m'manja ๐Ÿ˜‚

22/10/2024

Aaaaah a friend akuti matenda awo anawavera kukoma pamene akawatenga ๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…

22/10/2024

Palibe nyama yothamanga kwambiri ngat mkaz ophoda akamathawa vula ๐Ÿ’ƒ

22/10/2024

A traffic atakanika kupeza vuto la galimoto avekere magwelu amenewa bwanji ndewu ๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…๐Ÿ˜…

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gรชrรฃld Bรนllรค posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share