29/09/2024
tiseke limodzi๐๐
Nkazi wanga ndi ine timakangana koopsa
Nde ndikumuuza pakila katundu wako !!!__ ndisanamalize foni yake inayitana nde ndinamusiya kuti ayakhe foniyo. Anali bambo ake amvekere ndakutumizira 6 miliyoni 4 miliyoni uwapatse amunakowo ndiponso ndikutumiza range rover adzikwera atamaliza kucheza anadura foni kenaka anandiyang'ana ndikundifusa kuti paja umati ndi pakire ndidzitani
Mamuna: ndimati upakire dzovala zako ndikuchapire komanso kuyambira relo ndidzikuchapira ndine ๐ฐ๐จ .
๐๐๐
Amuna anakonza
๐๐๐
Chinde ndipangeni follow kapena like. Thanks for kuwerenga ๐๐
ndidzikuchapira ndine. ๐๐๐๐