Bwalo Tv

Bwalo Tv Entertainment, Education & politics
(1)

19/08/2026

Mphatso gumula ngati unalembera za escom kalata Yako anandimangila matemba zulo kubangwe😂

munthune ndayamba kusoka tipaseni ntchito yo tikupangilen
19/08/2026

munthune ndayamba kusoka tipaseni ntchito yo tikupangilen

16/08/2026

mkazi akamugulila mamuna chovala unva tavalani trouser nakugulilani ija🤣
apa ukananva tandipasileni chikho Cha wafcon🤣🤣🤣

16/08/2026

Ulipo lero Malawi vs Cameroon
Loselani zigoli

From inbox 📥neba wanga ndi family yake kma ine ndi bachala ndinamupepha kt nyumba yanga ndiyakulu mtsikana yekhayo azigo...
14/08/2026

From inbox 📥

neba wanga ndi family yake kma ine ndi bachala ndinamupepha kt nyumba yanga ndiyakulu mtsikana yekhayo azigona kunyumba kwanga kuli chipinda kma amakana Sono ndizimene akuchita apazi ndichilungamo 🤨🤨

 💔😭Wapezeka ataphedwa pafupi ndi bridge ya Chikonde ku Mulanje. Munthu yi sakudziwika kuti ndi ndani. Achipatala ndi a p...
14/08/2026


💔😭

Wapezeka ataphedwa pafupi ndi bridge ya Chikonde ku Mulanje. Munthu yi sakudziwika kuti ndi ndani. Achipatala ndi a police afika kuzanyamulapo thupi li

Kupangila amene samuziwa Tabitha and temwa chawinga 👍
14/08/2026

Kupangila amene samuziwa Tabitha and temwa chawinga 👍

Ambiri sakumuziwa player uyu 😂
14/08/2026

Ambiri sakumuziwa player uyu 😂

iwe ukugona ife tagula zotchipa😂😂😂
13/08/2026

iwe ukugona ife tagula zotchipa😂😂😂

sinankha azimayi athuwa 2027 waku world cup tizivala izizi basi
13/08/2026

sinankha azimayi athuwa 2027 waku world cup tizivala izizi basi

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bwalo Tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share