BCA Upcomming Artist

BCA Upcomming Artist NYASA LAND PICTURES

28/05/2022
30/04/2022

Try us
0990400334

26/04/2022

ONE SONG

Titakhala pasi taona Kuti ...aayii sizoona tiimilile .. poti kuKhala pasi ndi sign ya kutopa lol komaso taona kuti tisaimilile chabe koma Tiimilile Ghetto pobweletsa Njuchi ziwili panyimbo imodzi ..

imani kaye Njuchi imodzi mu Njuchi Zitatu ndi BEE PachiHiphop mumaziwa. TITLE yanyimboyi ikuyenela ikhale TITLE yoimililila chinthu chimodzi. Sitikutulutsa nyimbo ziwili .we are releasing Pa 2May ndimadalamadala Joy Nathu ..tune in your Madeonmonday this coming MONDAY



First drop This Year! Veda Njucci wakozeka?

26/04/2022

Eti bwanj✌️😀

Address

Blantyre

Telephone

+265883338833

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BCA Upcomming Artist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share