24/01/2026
wathu wa sabata ino
Dzina loimbira: Adolf Gidan
Dzina Lonse: Gideon Malinda
Tsiku lobadwira: 29 March 2002
Komwe akukhala: Mpemba
Kumudzi kochokera: Blantyre, Mpemba
Okwatira: Single
Mtundu wa anthu: Yao
Mbiri ya maphunziro: Diploma in public health certificate in tailoring and fashion designing
Chamba chomwe amaimba:
Oimba amene amawakonda mdera lino, mdziko muno komanso dziko lonse la pansi: KiDozi, Chisper-Namadingo, Gattah, Emmie Deebo, Gwamba, Classic, Yanos Central, Zeze- Makhadzi, 6xi9ine, Yo Maps, Diamond on his fashion, Eminem
Ndalama zomwe amapanga pa mwenzi: Depends since now am not financially stable
Chakudya chomwe amachikonda: Polk meat, chips ndiye pakhalenso kamowa wezi
Mbiri/chomwe chinamulimbikitsa kuyamba kuimba: poyamba ndinkakonda kumvera nyimbo kwambiri kenako ndinayamba kumayesera Kulemba zanga koma sindimkapita ku studio, Arthur Minyanga ku ZGSS ndamene anandilimbikitsa kuti ndikalowe studio atapeza ma lyric mu copy mwanga ndipo anawayamikira ngakhale sanali oyimba
Chomwe amafuna atakwaniritsa pa nkhani ya maimbidwe: Kufikira anthu Ambiri Malawi muno ndi kunja, kuwaphunzitsa, kuwasangalasa, ndi kuwadzudzula zomwe zidzaike Mpemba pa map, kunoko ndimafunitsitsa kutazachoka ma artist angapo otchuka mmene ilili Machinjiri, Bangwe, ndi Soche
Nyimbo yake ina: https://youtu.be/oC-XsKNJG0A?si=1_G2poJwF3JXilqK