Veer madron entertainment

Veer madron entertainment Don't fear to take a riske

21/05/2024

Ndikunena pano kupepesa kuli mkati kulila ndi kulila😭😭

Matamano kukacha amvekele sindipembeza mkaz🙄🙄

Simbani moyo neba

MAKOLO MULIKUTI ? ⚠️ Tatola mwanayu kuno ku Area 36 ati dzina ndi Grace kwao sakudziwa.   Tukamusiya kwa mfumu aChapata....
21/05/2024

MAKOLO MULIKUTI ? ⚠️

Tatola mwanayu kuno ku Area 36 ati dzina ndi Grace kwao sakudziwa. Tukamusiya kwa mfumu aChapata. Makolo komwe muliko imbani phone pa 0999932620.

 Tinali tikufufuzabe za ngozi yomwe yachitika pa Lizulu mawola angapo apitawa.Malingana ndi kafuku fuku yemwe tapanga ta...
21/05/2024



Tinali tikufufuzabe za ngozi yomwe yachitika pa Lizulu mawola angapo apitawa.

Malingana ndi kafuku fuku yemwe tapanga tapeza kuti chiwelengelo cha anthu omwalira sopano chafika pa atatu kuchoka pa awiri ndipo khumi ndi asanu 15 ndi omwe avulala.

Ngoziyi inakhunza anthu omwe amagulisa malonda pamalopo ndipo anthu awiri anamwalira pamalo pompo pomwe wina wamwalila akulandila thandizolo la chipatala.

Chazesa ngoziyi ndichakuti dalayiva wa Bus Matours analephela kuwongolela chifukwa cha kuthamanga kwambiri zomwe zinapangisa kuti akawombeToyota Hilux komaso anthu ena omwe amachita malonda pamalopo kuphatizaso ziweto.

Padakali pano anthu omwe avulalawa asanu akulandila thandizo la chipatala pa chipatala chachikukulu cha Dedza pomwe ena khumi atulusidwa.

Tiyeni tizipemphela mu uzimu ndi mchowonadi mulungu atithandize

K*ti mupange follow
Dinani apa 👉veer madron entertainment

19/05/2024
19/05/2024

Kuli wa moto lero pomwe Silver Strikers ikhale ikusewera ndi team ya Mighty Mukuru Wanderers pa bwalo la Silver mu TNM Super League 🏆

Satirani masewerowa online mukapanga Follow page yathu, mulikwanu pheee pachiSunday ndiokondedwa anu ma results kumangopezani👏
dinani apa K*t mumve zambiri madron entertainment #

17/05/2024

TAKE IT EASY
The pain of today
Shall be
The joy of Tommorow
In Jesus Name
🙏

11/05/2024

GOD'S PLAN
Is always beautiful
Than
Our desire
🙏

11/05/2024

When you turn your worries
Into worship
God will turn your battles
Into blessings
AMEN

11/05/2024

Khawa zimene mumalemba mkuika pa status
Mutamutulila Mlungu
Nyengo
Zanu zitha kusitha 😢😢

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Veer madron entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share