Sylvester Kalizang'oma

  • Home
  • Sylvester Kalizang'oma

Sylvester Kalizang'oma Sylvester Kalizang'oma is a vernacular poet and writer who builds worlds with words and expresses the unspoken through poetry.
(7)

08/06/2026

Kuposedwa mpikisano wothamanga ndi munthu yemwe amathamanga cha futambuyo

08/06/2026

Uyuyu akunena zoonaditu chifukwa mmm!! achinyamata tawonjeza, maka mabatchala mukayankha.

08/06/2026

"AKUTI MWINA BOLANSO TEMIK AMATHA KU KHURULUKA"
Watero Michael Benjala

08/06/2026

"Akazi andiyanja koma ndalama ndiribe"

-Watelo mkulu wina-

07/06/2026

Rearrange the letters; form the word:

A E D N S W E Y D

Tonde ndeuti apa?
07/06/2026

Tonde ndeuti apa?

Izizi zomati chikondi chili m'manja zi, n'kumapatsana moni wa chanza zi mmm!! zipume kaye bwa. Nanga n'kukhala uku?
07/06/2026

Izizi zomati chikondi chili m'manja zi, n'kumapatsana moni wa chanza zi mmm!! zipume kaye bwa. Nanga n'kukhala uku?

Atsikana awiri akakhala kuti amakondana ndipo amagwirizana kwambiri kapena kuti adakulirapo limodzi komanso nthawi zambi...
07/06/2026

Atsikana awiri akakhala kuti amakondana ndipo amagwirizana kwambiri kapena kuti adakulirapo limodzi komanso nthawi zambiri kulikonse amatha kumayendera limodzi.
Koma ngati pakati pa awiriwa m'modzi yekha akamafunsilidwa ndi anyamata pafupi pafupi pomwe winayo olo moni osalandira nkomwe mwina kamba kamwano wake, kudzimva shuga, kudziwona kukula subwoofer, akatumba komanso mahips.
Dziwani mtsikana amene amafunsilidwayu amasanduka m'dani wa mtsikana wosafunsiridwayo

07/06/2026

In war the heart must be sacrificed

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sylvester Kalizang'oma posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Establishment

Send a message to Sylvester Kalizang'oma:

  • Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment?

Share