01/11/2024
Breaking 🚨
Football Association of Malawi yasankha yemwe anali Coach wa FCB Nyasa Big Bullets Mr Kalisto Pasuwa kukhala coach ogwilizira wa Flames .
Izi zikudza kamba ka kusachita bwino kwa Coach Patrick Mabedi.
FAM yasankhaso a Peter Mponda , Kinna Phiri ndi ena ngati othandizira Pasuwa.
Kodi tsogolo la Flames ndilotani ndikusankhidwa kwa anthuwa?