Lexina Official

Lexina Official This is Official page for Lexina
(1)

Bambo anga amwalira Saturday koma uthenga wandipeza atayika kale Monday lapatili, ndadandaula kwambiri πŸ’”πŸ™ŒπŸ₯ΊπŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­
08/10/2026

Bambo anga amwalira Saturday koma uthenga wandipeza atayika kale Monday lapatili, ndadandaula kwambiri πŸ’”πŸ™ŒπŸ₯ΊπŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­

Eti Flynn akufanana ndi ndani? β€οΈπŸ™
08/10/2026

Eti Flynn akufanana ndi ndani? β€οΈπŸ™

Happy 1st birthday Flynn my brother β€οΈπŸŽ‰ khekhe udyaa weekend πŸ₯‚
07/10/2026

Happy 1st birthday Flynn my brother β€οΈπŸŽ‰ khekhe udyaa weekend πŸ₯‚

05/10/2026

Pa mzoma pa boma, Amoeba & my manager Fly P πŸ”₯πŸ”₯πŸ’―

Manager ❀️
05/10/2026

Manager ❀️

Dad β€οΈπŸ«‚
05/10/2026

Dad β€οΈπŸ«‚

Lazz G - Bayala ft Malima & Thom Dee now out πŸ“ΈπŸ”₯
05/10/2026

Lazz G - Bayala ft Malima & Thom Dee now out πŸ“ΈπŸ”₯

Directed by 0993906647

Nkhani yabwino Kwa azibale anga okhala ku Theba β€οΈπŸ˜πŸ«‚Nellie the transporter, mwana wanu yekhayo odalilika komaso wa mbiri...
03/10/2026

Nkhani yabwino Kwa azibale anga okhala ku Theba β€οΈπŸ˜πŸ«‚

Nellie the transporter, mwana wanu yekhayo odalilika komaso wa mbiri yabwino pa business akukumbutsani kuti musavutike kapena kuda nkhawa zakatumizidwe Wakatundu kuchoka ku South Africa kupita kumudzi ku Malawi.

Nellie transporters ikafika kuno ku mudzi ndi katundu wanu, imayenda door to door ndipo there is πŸ’―% assurance kuti wanu amafika yense komaso mu nthawi yake, ma phone number awo amakhala on 24hrs.

Tatipezeni lero kuti tipange business pa number iyi +265995620019 / 0677880548

Looking for dancers in Mzuzu, asap inbox me, if u are a good dancer and you looking for a exposure!! Weekend Yi tijambul...
01/10/2026

Looking for dancers in Mzuzu, asap inbox me, if u are a good dancer and you looking for a exposure!! Weekend Yi tijambula video yanga ya new one, amene amalakalaka ataonekako mu nyimbo yanga uwu ndi mwayi wanu.
What's app: 0888053905

01/10/2026

Lexina x Lazz G (Produced by Munie verse!!)

Are you ready for the Hit? πŸŽΆπŸ™ŒπŸ“ΈπŸ”₯

Address

Manchester

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lexina Official posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category